Luka 8

Akazi otumikira Yesu ndi cuma cao 1 Ndipo kunali, katapita kamphindi anayendayenda kumizinda ndi kumidzi, kulalikira ndi kuwauza U thenga Wabwino wa Ufumu wa Mulungu, ndi pamodzi naye khumi ndi…

Luka 9

Yesu atuma ophunzira ace kukalalikira mau 1 Ndipo iye anaitana pamodzi khumi ndi awiriwo nawapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse, ndi zakuciritsa nthenda. 2 Ndipo anawatuma kukalalikira Ufumu wa…

Luka 10

Yesu atuma ophunzira makumi asanu ndi awiri 1 Zitatha izi Ambuye anaika ena makumi asanu ndi awiri, nawatuma iwo awiri awiri pamaso pace ku mudzi uli wonse, ndi malo ali…

Luka 11

Pemphero la Ambuye 1 Ndipo kunali, pakukhala iye pamalo pena ndi kupemphera, m’mene analeka, wina wa ophunzira ace anati kwa iye, Ambuye, tiphunzitseni ife kupemphera, monganso Yohane anaphunzitsa ophunzira ace….

Luka 12

Yesu awacenjeza za cinyengo 1 Pomwepo pamene anthu a zikwi zikwi a khamu anasonkhana pamodzi, kotero kuti anapondana, iye anayamba kunena kwa ophunzira ace poyamba, Tacenierani nokha ndi cotupitsa mikate…

Luka 13

Maphedwe a Agalileya, tsanfa la Siloamu 1 Ndipo anakhalako nthawi yomweyo, anthu ena amene anamuuza iye za Agalileya, amene Pilato anasanganiza mwazi wao ndi nsembe zao. 2 Ndipo iye anayankha…

Luka 14

Yesu aciritsa munthu wodwala mbulu 1 Ndipo panali pamene iye analowa m’nyumba ya mmodzi wa akuru a Afarisi tsiku la Sabat a, kukadya, iwo analikumzonda iye. 2 Ndipo onani, panali…

Luka 15

Fanizo la nkhosa yosokera 1 Koma amisonkho onse ndi anthu ocimwa analikumyandikira kudzamva iye. 2 Ndipo Afarisi ndi alembi anadandaula nati, Uyu alandira anthu ocimwa, nadya nao. 3 Koma anati…

Luka 16

Fanizo la kapitao wonyenga 1 Ndipo iye ananenanso kwa ophunzira ace, Panali munthu mwini cuma, anali ndi kapitao wace; ndipo ameneyu ananenezedwa kwa iye kuti alikumwaza cuma cace. 2 Ndipo…

Luka 17

Za zolakwitsa, ndi makhululukidwe, ndi mphamvu ya cikhulupiriro ndi kutumikira kwathu 1 Ndipo anati kwa ophunzira ace, Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze; koma tsoka iye amene adza nazo. 2 Kukolowekedwa mwala…