Mateyu 22
Fanizo la ukwati 1 Ndipo Yesn anayankha, nalankhulanso kwa iwo m’mafanizo, nati, 2 Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wace phwando la ukwati, 3 natumiza akapolo…
Fanizo la ukwati 1 Ndipo Yesn anayankha, nalankhulanso kwa iwo m’mafanizo, nati, 2 Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wace phwando la ukwati, 3 natumiza akapolo…
Yesu adzudzula Alembi ndi Afarisi 1 Pomwepo Yesu analankhula ndi makamu a anthu ndi ophunzira ace, 2 nanena, Alembi ndi Afarisi akhala pa mpando wa Mose; 3 cifukwa cace zinthu…
Yesu anenera zam’tsogolo. Ciyambi ca masautso 1 Ndipo Yesu anaturuka kuKacisi; ndipo ophunzira ace anadza kudzamuonetsa cimangidwe ca Kacisiyo. 2 Koma Iye anayankha nati kwa iwo, Simuona izi zonse kodi?…
Fanizo la anamwali asanu ocenjera ndi asanu opusa 1 Pomwepo Ufumu wa Kumwamba udzafanizidwa ndi anamwali khumi, amene anatenga nyali zao, naturuka kukakomana ndi mkwati. 2 Ndipo asanu a iwo…
Akuru a Ayuda apangana amgwire Yesu 1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ace, 2 Mudziwa kuti akapita masiku awiri, Paskha ufika, ndipo Mwana wa…
Yudase adzipacika yekha 1 Ndipo pakudza mamawa, ansembe akuru ndi akuru a anthu onse anakhala upo wakumcitira Yesu, kuti amuphe; 2 ndipo anammanga Iye, namuka naye, nampereka Iye kwa Pilato…
Yesu auka kwa akufa 1 Ndipo popita dzuwa la Sabata, mbanda kuca, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Mariya wa Magadala, ndi Mariya winayo, kudzaona manda. 2 Ndipo onani, panali cibvomezi…
Yohane Mbatizi 1 CIYAMBI cace ca Uthenga Wabwino wa Yesu Kristu, Mwana wa Mulungu. 2 Monga mwalembedwa m’Yesaya mneneri, Ona, ndituma mthenga wanga patsogolo pa nkhope yanu, Amene adzakonza njira…
Aciritsa wodwala manjenje 1 Ndipo polowanso Iye m’Kapernao atapita masiku ena, kunamveka kuti ali m’nyumba. 2 Ndipo ambiri anaunjikana, kotero kuti anasowa malo, ngakhale pakhomo pomwe; ndipo analankhula nao mau….
Yesu aciritsa wa dzanja lopuwala 1 Ndipo analowanso m’sunagoge; ndipo munali munthu m’menemo ali ndi dzanja lace lopuwala. 2 Ndipo anamuyang’anira Iye, ngati adzamciritsa dzuwa la Sabata; kuti ammange mlandu….