Mateyu 12
Yesu mbuye wa Sabata 1 Nyengo imeneyo Yesu anapita tsiku la Sabata pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace anali ndi njala, nayamba kubudula ngala, nadya. 2 Koma Afarisi,…
Yesu mbuye wa Sabata 1 Nyengo imeneyo Yesu anapita tsiku la Sabata pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace anali ndi njala, nayamba kubudula ngala, nadya. 2 Koma Afarisi,…
Fanizo la Wofesa 1 Tsiku lomwelo Yesu anaturuka m’nyumbamo, nakhala pansi m’mbali mwa nyanja. 2 Ndipo makamu ambiri a anthu anasonkhanira kwa Iye, kotero kuti Iye analowa m’ngalawa, nakhala pansi,…
Herode amupha Yohane Mbatizi 1 Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu, 2 nanena kwa anyamata ace, U yo ndiye Yohane Mbatizi; anauka kwa akufa; ndipo cifukwa ca ici…
Miyambo ya makolo 1 Pomwepo anadza kwa Yesu Afarisi ndi alembi, ocokera ku Yerusalemu, nati, 2 Ophunzira anu alumphiranji miyambo ya makolo? pakuti sasamba manja pakudya. 3 Ndipo Iye anayankha,…
Afarisi ndi Asaduki afuna cizindikilo 1 Ndipo Afarisi ndi Asaduki anadza, namuyesa, namfunsa Iye awaonetse cizindikiro ca Kumwamba. 2 Koma Iye anayankha, nati kwa iwo, Madzulo munena, Kudzakhala ngwe; popeza…
Mawalitsidwe a Yesu paphiri 1 Ndipo atapita masiku asanu ndi limodzi, Yesu anatenga Petro, ndi Yakobo, ndi Yohane mbale wace, napita nao pa okha pa phiri lalitari; 2 ndipo Iye…
Wamkuru m’Ufumu wa Kumwamba 1 Nthawi yomweyo ophunzira anadza kwa Yesu, nanena, Ndani kodi ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba? 2 Ndipo pamene Yesu anaitana kamwana, anakaimitsa pakati pao, 3…
Za kalata wa cilekaniro 1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anacokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordano. 2 Ndipo makamu akuru…
Fanizo la anchito olembedwa mwina mwina 1 Pakuti Ufumu wa Kumwamba ufanana ndi munthu mwini banja, amene anaturuka mamawa kuka lembera anchito a m’munda wace wampesa. 2 Ndipo parnene adapangana…
Yesu alowa m’Yerusalemu 1 Ndipo parnene iwo anayandikira ku Yerusalemu, nafika ku Betefage, ku phiri la Azitona, pamenepo Yesu anatumiza ophunzira awiri, 2 nanena kwa iwo, Mukani ku mudzi wopenyana…