Mateyu 2

Anzeru a kummawa 1 Ndipo pa kubadwa kwace kwa Yesu m’Betelehemu wa Yudeya m’masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum’mawa anafika ku Yerusalemu, 2 nati, Ali kuti amene anabadwa…

Mateyu 3

Yohane Mbatizi 1 Ndipo masiku aja anadza Yohane Mbatizi, nalalikira m’cipululu ca Yudeya, 2 nanena, Tembenukani mitima; cifukwa Ufumu wa Kumwamba wayandikira. 3 Pakuti uyu ndiye ananenayo Yesaya mneneri, kuti,…

Mateyu 4

Yesu ayesedwa mcipululu 1 Pamenepo Yesu anatengedwa ndi Mzimu kumka kucipululu kukayesedwa ndi mdierekezi. 2 Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pace anamva njala….

Mateyu 5

Ciphunzitso ca paphiri Madalitso 1 Ndipo m’mene Iye anaona makamu, anakwera m’phiri; ndipo m’mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ace; 2 ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati: 3…

Mateyu 6

Za zopereka zacifundo; za kupemphera za kudzikana kudya 1 Yang’anirani kuti musacite zolungama zanu pamaso pa anthu kuti muonekere kwa iwo; pakuti ngati mutero mulibe mphotho ndi Atate wanu wa…

Mateyu 7

Za kuweruza mnzace, kulimbika m’kupemphera, zipata ziwiri, aneneri onyenga kumva ndi kucita 1 Musaweruze, kuti mungaweruzidwe. 2 Pakuti ndi kuweruza kumene muweruza nako, inunso mudzaweruzidwa; ndipo ndi muyeso umene muyesa…

Mateyu 8

Yesu aciritsa wakhate 1 Ndipo pakutsika pace paphiripo, inamtsata mipingo yambiri ya anthu. 2 Ndipo onani, wakhate anadza namgwadira Iye, nanena, Ambuye ngati mufuna mungathe kundikonza. 3 Ndipo Yesu anatambalitsa…

Mateyu 9

Munthu wamanfenje wa ku Kapernao 1 Ndipo Iye analowa m’ngalawa, naoloka, nadza kumudzi kwao. 2 Ndipo onani, anabwera naye kwa Iye munthu wamanjenje, wakugona pachika: ndipo Yesu pakuona cikhulupiriro cao,…

Mateyu 10

Atumwi khumi ndi awiri ndi utumiki wao 1 Ndipo pamene Iye anadziitanira ophunzira ace khumi ndi awiri, anapatsa iwo mphamvu pa mizimu yoipa, yakuiturutsa, ndi yakuciza nthenda iri yonse ndi…

Mateyu 11

Otumidwa ndi Yohane Mbatizi 1 Ndipo panali, pamene Yesu anatha kuwafotokozera ophunzira ace khumi Ndi awiri, Iye anacokera kumeneko kukaphunzitsa Ndi kulalikira m’midzi mwao. 2 Koma Yohane, pakumva m’nyumba yandende…