Zekariya 10
Malonjezo a kwa Israyeli 1 Pemphani kwa Yehova mvula, m’nyengo ya mvula ya masika, kwa Yehova wolenga mphezi; ndipo adzawapatsa mibvumbi ya mvula, kwayense zophukira kuthengo. 2 Pakuti aterafi anena…
Malonjezo a kwa Israyeli 1 Pemphani kwa Yehova mvula, m’nyengo ya mvula ya masika, kwa Yehova wolenga mphezi; ndipo adzawapatsa mibvumbi ya mvula, kwayense zophukira kuthengo. 2 Pakuti aterafi anena…
Kulangidwa kwa osalapa 1 Tsegula pa makomo ako Lebano, kuti moto uthe mikungudza yako. 2 Cema, mtengo wamlombwa, pakuti mkungudza wagwa, popeza mitengo yokoma yaipitsidwa; cemani athundu a ku Basani,…
Ukulu wa Israyeli m’tsogolo 1 Katundu wa mau a Yehova wakunena Israyeli. Atero Yehova, wakuyala miyamba, ndi kuika maziko a dziko lapansi, ndi kulenga mzimu wa munthu m’kati mwace; 2…
Kuyeretsedwa kwa Yerusalemu 1 Tsiku lomwelo padzatsegukira nyumba ya Davide ndi okhala m’Yerusalemu kasupe wa kwa ucimo ndi cidetso. 2 Ndipo kudzacitika tsiku lomwelo, ati Yehova wa makamu, ndidzaononga maina…
Yehova adzathandiza a ku Yerusalemu polimbana ndi amitundu 1 Taonani likudza tsiku la Yehova, limene zofunkha zako zidzagawanika pakati pako. 2 Pakuti ndidzasonkhanitsa amitundu onse alimbane ndi Yerusalemu; ndipo mudziwo…
Kusayamika kwa Israyeli pa cikondi ca Mulungu 1 KATUNDU wa mau a Yehova wa kwa Israyeli mwa Malaki. 2 Ndakukondani, ati Yehova; koma inu mukuti, Mwatikonda motani? Esau si mkulu…
Mau akutsutsa ansembe 1 Ndipo tsono, ansembe inu, lamulo ili ndi la kwa inu. 2 Mukapanda kumvera, mukapanda kuliika mumtima mwanu, kupatsa dzina langa ulemerero, ati Yehova wa makamu, ndidzakutumizirani…
Za mthenga wokonzeratu njira ya Ambuye 1 Taonani, ndituma mthenga wanga, kuti akonzeretu njira pamaso panga; ndipo Ambuye amene mumfuna adzadza ku Kacisi wace modzidzimutsa; ndiye mthenga wa cipangano amene…
Oipa adzalangidwa, okoma adzadalitsidwa. Asamale cilamulo; adzafika Eliya 1 Pakuti taonani, likudza tsiku, lotentha ngati ng’anjo; ndipo onse akudzikuza ndi onse akucita coipa, adzakhala ngati ciputu; ndi tsiku lirinkudza lidzawayatsa,…
Makolo a Yesu Kristu monga mwa thupi 1 BUKU la kubadwa kwa Yesu Kristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu. 2 Abrahamu anabala Isake; ndi Isake anabala Yakobo; ndi Yakobo…