Hagai 2

Ulemerero wa Kacisi waciwiri 1 Mwezi wacisanu ndi ciwiri, tsiku la makumi awiri ndi cimodzi la mweziwo, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti, 2 Unenetu kwa Zerubabele,…

Zekariya 1

Mneneri adandaulira anthu Ayuda aleke zoipa zao 1 MWEZI wacisanu ndi citatu, caka caciwiri ca Dariyo, mau a Yehova anadza kwa Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido mneneri, ndi…

Zekariya 2

Masomphenya acitatu: Yerusalemu ayesedwa ndi cingwe 1 Ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, ndipo taonani, munthu ndi cingwe coyesera m’dzanja lace. 2 Ndipo ndinati, Upita kuti? Ndipo anati kwa ine, Kukayesa Yerusalemu,…

Zekariya 3

Masomphenya acinai: Satana atsutsana ndi Yoswa, Mulungu amuyesa wolungama 1 Pamenepo anandionetsa Yoswa mkulu wa ansembe alikuima pamaso pa mthenga wa Yehova, ndi Satana alikuima pa dzanja lace lamanja, atsutsana…

Zekariya 4

Masomphenya acisanu: coikapo nyali cagolidi ndi nyali zace 1 Ndipo mthengayo adalankhula nane, anadzanso, nandiutsa ngati munthu woutsidwa m’tulo tace. 2 Ndipo anati kwa ine, Uona ciani? Ndipo ndinati, Ndaona,…

Zekariya 5

Masomphenya acisanu ndi cimodzi: mpukutu wouluka 1 Pamenepo ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, taonani, mpukutu wouluka. 2 Ndipo anati kwa ine, Uona ciani? Ndipo ndinayankha, Ndiona mpukutu wouluka; utali wace mikono…

Zekariya 6

Masomphenya acisanu ndi citatu: magareta anai 1 Ndipo ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, ndipo taonani, anaturuka magareta anai pakati pa mapiri awiri; ndi mapiriwo ndiwo mapiri amkuwa. 2 Ku gareta woyamba…

Zekariya 7

Kusala kosalamulidwa ndi Yehova 1 Ndipo kunacitika caka cacinai ca mfumu Dariyo, mau a Yehova anadza kwa Zekariya tsiku lacinai la mwezi wacisanu ndi cinai, ndiwo Kisilevi. 2 Ndipo a…

Zekariya 8

Madalitso olonjezedwa ndi Mulungu 1 Ndipo mau a Yehova wa makamui anadza kwa ine, ndi kuti, 2 Atero Yehova wa makamu: Ndimcitira nsanje Ziyoni ndi nsanje yaikuru, ndipo ndimcitira nsanje…

Zekariya 9

Kulangidwa kwa amitundu ena 1 Katundu wa mau a Yehova pa dziko la Hadraki, ndipo Damasiko adzakhala popumula pace; pakuti Yehova apenyerera anthu monga apenyerera mafuko onse a Israyeli; 2…