Nahumu 1

Cilungamo ndi cifundo ca Mulungu. Adzaononga adani ndi kulanditsa anthu ace 1 KATUNDU wa Nineve. Buku la masomphenya a Nahumu wa ku Elikosi. 2 Yehova ndiye Mulungu wansanje, nabwezera cilango;…

Nahumu 2

Nineve amangidwa misasa nalandidwa 1 Wophwanyayo wakwera pamaso pako; sunga linga, yang’anira panjira, limbitsa m’cuuno mwako, limbikitsatu mphamvu yako. 2 Pakuti Yehova abwezeranso ukulu wace wa Yakobo ngati ukulu wace…

Nahumu 3

Zoipa za Nineve ndi kupasuka kwace 1 Tsoka mudzi wa mwazi! udzala nao mabodza ndi zacifwamba; zacifwamba sizidukiza. 2 Kumveka kwa cikoti, ndi mkokomo wa kuyenda kwa njinga za magareta;…

Habakuku 1

Cisalungamo ca Ayuda. Akasidi adzawadzera ndi kuononga zonse. Mneneri apempherera Ayuda 1 KATUNDU adamuona Habakuku 2 Yehova, ndidzapfuula mpaka liti osamva Inu? ndipfuulira kwa Inu za ciwawa, koma simupulumutsa. 3…

Habakuku 2

Akasidi omwe adzalangidwa 1 Ndidzaima pa dindiro langa ndi kudziika palinga, ndipo ndidzayang’anira ndione ngati adzanenanji mwa ine, ngatinso ndidzamyankha ciani pa coneneza canga. 2 Ndipo Yehova anandiyankha nati, Lembera…

Habakuku 3

Pemphero la Habakuku 1 Pemphero la Habakuku mneneri, pa Sigionoto. 2 Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha; Yehova, tsitsimutsani nchito yanu pakati pa zaka, Pakati pa zaka mudziwitse; Pa mkwiyo…

Zefaniya 1

Mau oopsa akucenjeza Yerusalemu ndi Yuda 1 MAU a Yehova amene anadza kwa Zefaniya mwana wa Kusi, mwana wa Gedaliya, mwana wa Amariya, mwana wa Hezekiya, masiku a Yosiya, mwana…

Zefaniya 2

Mau akucenjeza amitundu ena 1 Dzisanthuleni, inde santhulani; inu mtundu wosakhumba kanthu; 2 lamulo lisanabale, tsiku lisanapitirire ngati mungu, usanakugwereni mkwiyo waukali wa Yehova, lisanakugwereni tsiku la mkwiyo wa Yehova….

Zefaniya 3

Mau akudzudzula Yerusalemu. Malonjezo a kwa okhulupirika otsala 1 Tsoka uyo wopanduka, ndi wodetsedwa, ndiye mudzi wozunza! 2 Sanamvera mau, sanalola kulangizidwa; sanakhulupirira Yehova, sanayandikira kwa Mulungu wace. 3 Akalonga…

Hagai 1

Mau akudzudzula ndi kudandaulira Ayuda amangenso Kacisi 1 CAKA caciwiri ca mfumu Dariyo, mwezi wacisanu ndi cimodzi, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri kwa Zerubabele mwana wa Sealitiyeli, ciwanga…