Yona 2
Pemphero la Yona ali m’mimba mwa cinsomba 1 Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wace ali m’mimba mwa nsombayo. 2 Ndipo anati, Ndinaitana Yehova m’nsautso yanga, Ndipo anandiyankha ine; Ndinapfuula…
Pemphero la Yona ali m’mimba mwa cinsomba 1 Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wace ali m’mimba mwa nsombayo. 2 Ndipo anati, Ndinaitana Yehova m’nsautso yanga, Ndipo anandiyankha ine; Ndinapfuula…
Yona ku Nineve, Kulapa kwa a ku Nineve 1 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yona nthawi yaciwiri, ndi kuti, 2 Nyamuka, pita ku Nineve mudzi waukuru uja, nuulalikire uthenga…
Kudandaula kwa Yona, kumdzudzula kwa Mulungu 1 Koma sikudakomera Yona konse, ndipo anapsa mtima. 2 Ndipo anapemphera kwa Yehova, nati, Ha, Yehova! si ndiwo mau anga ndikali m’dziko langa? cifukwa…
Mau akucenjeza lsrayeli ndi Yuda cifukwa ca macimo ao 1 MAU a Yehova amene anadza kwa Mika wa ku Morese masiku a Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, amene adaona za Samariya…
Mau akutsutsa akulanda za eni 1 Tsoka iwo akulingirira cinyengo, ndi kukonza coipa pakama pao! kutaca m’mawa acicita, popeza cikhozeka m’manja mwao. 2 Ndipo akhumbira minda, nailanda; ngakhale nyumba, nazicotsa;…
Cilangizo ca Mulungu cifukwa ca atsogoleri ndi aneneri onyenga 1 Ndipo ndinati, Imvanitu, inu akuru a Yakobo, ndi oweruza a nyumba ya Israyeli; simuyenera kodi kudziwa ciweruzo? 2 inu amene…
Kuitanidwa kwa amitundu 1 Koma kudzacitika masiku otsiriza, kuti phiri la nyumba ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa mapiri, nilidzakuzika pamwamba pa zitunda; ndi mitundu ya anthu idzayendako. 2 Ndipo amitundu…
1 Uzisonkhana tsopano magulu magulu, mwana wamkazi wa magulu iwe; watimangira misasa, adzapanda woweruza wa Israyeli ndi ndodo patsaya. Aneneratu za kubadwa kwa woweruza m’Israyeli 2 Koma iwe, Betelehemu Efrata,…
Mulungu atsutsana ndi anthu ace cifukwa ca zoipa zao 1 Tamverani tsono conena Yehova: Nyamuka, tsutsana nao mapiri, ndi zitunda zimve mau ako. 2 Tamvani, mapiri inu, citsutsano ca Yehova,…
Za kuipa kwakukuru kwa Aisrayeli, ndi cifundoca Mulungu 1 Kalanga ine! pakuti ndikunga atapulula zipatso za m’mwamvu, atakunkha m’munda wamphesa; palibe mphesa zakudya; moyo wanga ukhumba nkhuyu yoyamba kupsa. 2…