Eksodo 31

1 Za amisiri opanga nchitoyi, Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Taona ndaitana ndi kumchula dzina lace, Bezaleli, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa pfuke la Yuda;…

Eksodo 32

Fano la mwana wa ng’ombe 1 Koma pamene anaona kuti Mose anacedwa kutsika m’phiri, anthuwo anasonkhana kwa Aroni, nanena naye, Ukani, tipangireni milungu yakutitsogolera; pakuti Mose uyu, munthuyu anatikweza kucokera…

Eksodo 33

Mulungu akuti sadzawaperekezanso 1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Muka, kwera kucokera kuno, iwe ndi anthu amene unawakweza kucokera m’dziko la Aigupto, kumka ku dzikolo ndinalumbirira nalo Abrahamu, ndi Isake,…

Eksodo 34

Magome atsopano a Malamulowo 1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Dzisemere magome awiri amiyala onga oyamba aja; ndipo ndidzalembera pa magomewo mau omwewo anali pa magome oyambawo, amene unawaswa. 2…

Eksodo 35

Zopereka zofunika za pa cihemaco 1 Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israyeli, nanena nao, Siwa mau amene Yehova anauza, kuti muwacite. 2 Masiku asanu ndi limodzi azigwira…

Eksodo 36

Pamenepo anacita Bezaleli ndi 1 Aholiabu, ndi anthu aluso, amene Yehova adaika luso ndi nzeru m’mtima mwao adziwe macitidwe ace a nchito yonse ya utumiki wace wa malo opatulika, monga…

Eksodo 37

Mapangidwe a likasa 1 Ndipo Bezaleli anapanga likasa la mtengo wasitimu; utali wace mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwace mkono ndi hafu, ndi msinkhu wace mkono ndi hafu; 2…

Eksodo 38

Mapangidwe a guwa la nsembe yopsereza 1 Ndipo anapanga guwa la nsembe yopsereza la mtengo wasitimu; utali wace mikono isanu, ndi kupingasa kwace mikono isanu, lampwamphwa; ndi msinkhu wace mikono…

Eksodo 39

Maombedwe a zobvala za ansembe 1 Ndipo anaomba zobvala zakutumikira nazo ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, atumikire nazo m’malo opatulika, naomba zobvala zopatulika za Aroni; monga Yehova adamuuza Mose….

Eksodo 40

Mose autsa cihemaco 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Tsiku loyamba la mwezi woyamba ukautse kacisi wa cihema cokomanako. 3 Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nucinge likasalo…