Amosi 2
1 Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Moabu, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatentha mafupa a mfumu ya ku Edomu asanduke njereza; 2 koma ndidzatumiza moto pa Moabu,…
1 Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Moabu, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatentha mafupa a mfumu ya ku Edomu asanduke njereza; 2 koma ndidzatumiza moto pa Moabu,…
Zoipa za Israyeli; aneneratu kuti adzalangidwa 1 Tamverani mau awa akunenerani Yehova motsutsa, inu ana a Israyeli, kulinenera banja lonse ndinalikweza kuliturutsa m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2 Inu nokha…
Aisrayeli adzadulidwa cifukwa ca zoipa ndi kuuma mtima kwao 1 Tamverani mau awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana, zokhala m’phiri la Samariya, zosautsa aumphawi, zopsinja osowa, zonena kwa ambuyao,…
Nyimbo ya maliro yakunena za kutyoka kwa Israyeli 1 Tamverani mau awa ndinenawa, akhalire inu nyimbo ya maliro, nyumba ya Israyeli inu. 2 Namwali wa Israyeli wagwa, sadzaukanso; wagwetsedwa pa…
Aisrayeli otsata zilakolako zao adzapsinjika ndi mtundu wina wa anthu 1 Tsoka osalabadirawo m’Ziyoni, ndi iwo okhazikika m’phiri la Samariya, ndiwo anthu omveka amtundu woposa wa anthu, amene nyumba ya…
Masomphenya atatu, dzombe, moto wonyambita, ndi cingwe: colungamitsa ciriri 1 Ambuye Yehova anandionetsa cotere; ndipo taonani, anaumba dzombe, poyamba kuphuka kwa maudzu a cibwereza; ndipo taonani, ndico cibwereza atawasengera mfumu….
Masomphenya a mtanga wa zipatso, Zoopsa za pa Israyeli 1 Ambuye Yehova anandionetsa cotere; ndipo taonani, mtanga wa zipatso zamalimwe. 2 Ndipo anati, Amosi uona ciani? Ndipo ndinati, Mtanga wa…
Masomphenya a kulangidwa koopsa. Lonjezo kuti madalitso adzabwera 1 Ndinaona Ambuye alikuima pa guwa la nsembe, nati Iye, Kantha mitu ya nsanamira, kuti ziundo zigwedezeke; nuphwanye mitu yao yonse; ndipo…
Zoipa zao ndi kulangidwa kwa Aedomu. Dalo la Israyeli 1 MASOMPHENYA a Obadiya. Atero Ambuye Yehova za Edomu: Tamva mbiri yocokera kwa Yehova, ndi mthenga wotumidwa mwa amitundu, ndi kuti,…
Kuitanidwa kwa Yona, kuthawa kwace, ndi kulangidwa kwace 1 NDIPO mau a Yehova anadza kwa Yona mwana wa Amitai, ndi kuti, 2 Nyamuka, pita ku Nineve, mudzi waukuruwo, nulalikire motsutsana…