Danieli 1

Maleredwe a Danieli ndi anzace kwa mfumu ya ku Babulo 1 CAKA cacitatu ca Yehoyakimu mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo adadza ku Yerusalemu, naumangira misasa ya nkhondo….

Danieli 2

Nebukadinezara alota, Danieli ammasulira lotolo 1 Caka caciwiri ca Nebukadinezara mfumu, Nebukadinezarayo analota maloto, ndi mzimu wace unabvutika, ndi tulo tace tidamwazikira. 2 Pamenepo mfumu inauza munthu aitane alembi, ndi…

Danieli 3

Nebukadinezara apanga fano lagolidi 1 Mfumu Nebukadinezara anapanga fano lagolidi, msinkhu wace mikono makumi asanu ndi limodzi, ndi thunthu lace mikono isanu ndi umodzi; analiimika pa cidikha ca Dura, m’dera…

Danieli 4

Loto la Nebukadinezara la mtengo waukuru 1 Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu, mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala pa dziko lonse lapansi: Mtendere ucurukire inu. 2 Candikomera kuonetsa zizindikilo ndi…

Danieli 5

Madyerero a Belisazara, dzanja lolemba pakhoma 1 Mfumu Belisazara anakonzera anthu ace akulu cikwi cimodzi madyerero akuru, namwa vinyo pamaso pa cikwico. 2 Belisazara, pakulawa vinyo, anati abwere nazo zotengera…

Danieli 6

Akalonga amchulira Danieli cifukwa kwa Dariyo 1 Kudamkomera Dariyo kuikira ufumuwo akalonga zana limodzi mphambu makumi awiri akhale m’madera onse a ufumu; 2 ndi akuyang’anira iwo akulu atatu, woyamba wao…

Danieli 7

Masomphenya a Danieli a zamoyo zinai ndi Nkhalamba ya kale lomwe 1 Caka coyamba ca Belisazara mfumu ya ku Babulo Danieli anaona loto, naona masomphenya a m’mtima mwace pakama pace;…

Danieli 8

Masomphenya a nkhosa yamphongo ndi tonde 1 Caka cacitatu ca Belisazara mfumu masomphenya anandionekera kwa ine Danieli, atatha kundionekera oyamba aja. 2 Ndipo ndinaona m’masomphenya; tsono kunali, pakuwaona ine ndinali…

Danieli 9

Pemphero la Danieli 1 Caka coyamba ca Dariyo mwana wa Ahaswero, wa mbeu ya Amedi, amene anamlonga mfumu ya Akasidi; 2 caka coyamba ca ufumu wace, ine Danieli ndinazindikira mwa…

Danieli 10

Danieli aona masomphenya oopsa, mngelo amlimbikitsa 1 Caka cacitatu ca Koresi mfumu ya Perisiya, cinabvumbulutsidwa cinthu kwa Danieli, amene anamucha Belitsazara; ndipo cinthuco ncoona, ndico nkhondo yaikuru; ndipo anazindikira cinthuco,…