Ezekieli 39
1 Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, nenera motsutsana naye Gogi, uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe Gogi, iwe mfumu yaikuru ya Meseki ndi Tubala; 2 ndipo ndidzakutembenuza, ndi kukutsogolera,…
1 Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, nenera motsutsana naye Gogi, uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe Gogi, iwe mfumu yaikuru ya Meseki ndi Tubala; 2 ndipo ndidzakutembenuza, ndi kukutsogolera,…
Masomphenya a Ezekieli, kukonzekanso kwa Kacisi ndi mabwalo ace 1 Caka ca makumi awiri ndi zisanu ca undende wathu, poyamba caka, tsiku lakhumi lamwezi, caka cakhumi ndi zinai atakantha mudziwo,…
Kukonzekanso kwa Kacisi: malo opatulikitsa 1 Ndipo anadza nane ku Kacisi, nayesa nsanamira zace, kupingasa kwace mikono isanu ndi umodzi cakuno, ndi mikono isanu ndi umodzi cauko, ndiko kupingasa kwa…
Kukonzekanso kwa Kacisi: zipinda zopatulika 1 Pamenepo anaturuka nane kumka ku bwalo la kunja, njira ya kumpoto; nalowa nane ku nyumba yazipinda idali pandunji pa mpatawo, ndi pandunji pa nyumbayo…
Kukonzekanso kwa Kacisi: ulemerero wa Mulungu 1 Pamenepo anamuka nane ku cipata coloza kum’mawa, 2 ndipo taonani, ulemerero wa Mulungu wa Israyeli unadzera njira ya kum’mawa, ndi mau ace ananga…
Kukonzekanso kwa Kacisi: utumiki wa Alevi ndi ansembe 1 Pamenepo anandibweza njira ya ku cipata cakunja ca malo opatulika coloza kum’mawa, koma cinatsekedwa. 2 Ndipo Yehova anati kwa ine, Cipata…
Cigawo ca dziko 1 Ndipo pogawa dziko likhale calowa cao, mupereke copereka kwa Yehova, ndico gawo lopatulika la dziko; m’litali mwace likhale la mabango zikwi makumi awiri mphambu zisanu, ndi…
Za Sabata ndi pokhala mwezi 1 Atero Ambuye Yehova, Pa cipata ca bwalo lam’kati coloza kum’mawa patsekedwe masiku asanu ndi limodzi ogwira nchito; koma tsiku la Sabata patsegulidwe, ndi tsiku…
Masomphenya a madzi oturuka m’Kacisi watsopano 1 Ndipo anandibwezera ku khomo la nyumba, ndipo taonani, panatumphuka madzi pansi pa ciundo ca nyumba kum’mawa; pakuti khomo lace la nyumba linaloza kum’mawa;…
Magawidwe a dziko mwa mafuko khumi ndi awiri 1 Maina a mafuko tsono ndi awa: Kuyambira nsonga ya kumpoto, ku mbali ya njira ya ku Heteloni, polowera ku Hamati, Hazarenani…