Ezekieli 29

Aneneratu za kulangidwa kwa Aigupto 1 Caka cakhumi, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi ndi ciwiri la mweziwo, anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa: nkhope yako itsutsane…

Ezekieli 30

Aigupto adzagonjetsedwa ndi mfumu ya ku Babulo 1 Anandidzeranso mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, nenera, uziti, Atero Ambuye Yehova, Liritsani, Ha, tsikulo 3 Pakuti layandikira tsiku,…

Ezekieli 31

Mau ena oneneratu za Farao 1 Ndipo kunali caka cakhumi ndi cimodzi, mwezi wacitatu, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, nena kwa…

Ezekieli 32

Nyimbo ya maliro ya pa Farao 1 Ndipo kunali caka cakhumi ndi ciwiri, mwezi wakhumi ndi ciwiri, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu…

Ezekieli 33

Udindo wa mneneri 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Nena ndi ana a anthu a mtundu wako, uziti nao, Ndikafikitsira dziko liri lonse lupanga,…

Ezekieli 34

Aneneratu motsutsa abusa osakhulupirika a anthu a Mulungu 1 Ndipo mau a Yehova anandidzera, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Nenera motsutsa abusa a Israyeli; nenera, nuti nao abusawo, Atero…

Ezekieli 35

Aneneratu za kulangidwa kwa a ku phiri la Seiri 1 Nandidzeranso mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Lozetsa nkhope yako ku phiri la Seiri, nulinenere molitsutsa; 3…

Ezekieli 36

Aneneratu za mapiri a Israyeli 1 Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, unenere kwa mapiri a Israyeli, uziti, Mapiri a Israyeli inu, imvani mau a Yehova. 2 Atero Ambuye Yehova, Popeza…

Ezekieli 37

Masomphenya a mafupa 1 Dzanja la Yehova linandikhalira, ndipo anaturuka nane mu mzimu wa Yehova, nandiika m’kati mwa cigwa, ndico codzala ndi mafupa; 2 ndipo anandipititsa pamenepo pozungulira ponse, ndipo…

Ezekieli 38

Anereratu za kulangidwa kwa Gogi 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako kwa Gogi, wa ku dziko la Magogi, ndiye mfumu yaikuru…