Ezekieli 19
Fanizo la mkango waukazi, ndi la mpesa 1 Ndipo iwe, takwezera akalonga a Israyeli nyimbo ya maliro, 2 uziti, Mai wako ndi ciani? Mkango waukazi unabwanthama mwa mikango, unalera ana…
Fanizo la mkango waukazi, ndi la mpesa 1 Ndipo iwe, takwezera akalonga a Israyeli nyimbo ya maliro, 2 uziti, Mai wako ndi ciani? Mkango waukazi unabwanthama mwa mikango, unalera ana…
Macimo a Aisrayeli citurukire iwo m’dziko la Aigupto 1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi ciwiri, mwezi wacisanu; tsiku lakhumi la mwezi, anadza akulu ena a Israyeli kufunsira kwa Yehova, nakhala…
Lupanga la Yehova 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku Yerusalemu, nuwabenthulire mau malo opatulikawa, nunenere dziko la Israyeli kulitsutsa; 3…
Macimo oopsa a Yerusalemu 1 Anandidzeransomau a Yehova, akuti, 2 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzaweruza, udzauweruza mudziwo wa mwazi kodi? uudziwitse tsono zonyansa zace zonse. 3 Nuziti, Atero Ambuye…
Ohola ndi Oholiba acigololowo 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, panali akazi awiri, mai wao ndi mmodzi; 3 ndipo anacita cigololo iwo m’Aigupto, anacita…
Fanizo la mphika wobwadamuka 1 Anandidzeranso mau a Yehova caka cacisanu ndi cinai, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi la mwezi, ndi kuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Udzilembere dzina la tsiku…
Aneneratu za kulangidwa kwa Aamoni 1 Ndipo mau a Yehova anandidzera, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Lozetsa nkhope yako kwa ana a Amoni, nuwanenere; 3 nunene kwa ana a…
Za kulangidwa kwa Turo 1 Ndipo kunali caka cakhumi ndi cimodzi, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, popeza Turo ananyodola Yerusalemu, ndi…
Nyimbo ya maliro ya pa Turo 1 Anandidzeranso mau a Yehova, akuti, 2 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, Takwezera Turo nyimbo ya maliro; 3 nuti kwa Turo, Iwe wakukhala polowera…
Aneneratu za kulangidwa kwa mfumu ya ku Turo 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, uziti kwa kalonga wa Turo, Atero Ambuye Yehova, Popeza mtima…