Yeremiya 46

Aneneratu kuti mfumu ya ku Babulo idzagonjetsa Aaigupto 1 Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya mneneri akunena za amitundu. 2 Za Aigupto: kunena za nkhondo ya Farao-neko mfumu ya…

Yeremiya 47

Aneneratu za citsutso ca Afilisti 1 Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya mneneri onena za Afilisti, Farao asanakanthe Gaza. 2 Yehova atero: Taonani, madzi adzakwera kuturuka kumpoto, nadzakhala mtsinje…

Yeremiya 48

Citsutso ca Moabu 1 Za Moabu Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Tsoka Nebo! pakuti wapasuka; Kiriyataimu wacitidwa manyazi, wagwidwa; linga la pamtunda lacitidwa manyazi lapasudwa. 2 Palibenso kutamanda…

Yeremiya 49

Citsutso ca Aamoni 1 Za ana a Amoni. Yehova atero: Kodi Israyeli alibe ana amuna? alibe wolowa dzina? M’mwemo mfumu yao yalowa pa Gadi cifukwa canji, ndi anthu ace akhala…

Yeremiya 50

Citsutso ca Babulo 1 Mau amene ananena Yehova za Babulo, za dziko la Akasidi, mwa Yeremiya mneneri. 2 Lalikirani mwa amitundu, falikitsani, kwezani mbendera; falikitsani, musabise; munene, Babulo wagwidwa, Beli…

Yeremiya 51

1 Yehova atero: Taonani, ndidzaukitsira Babulo, ndi iwo okhala m’Lebi-kamai, mphepo yoononga, 2 Ndipo ndidzatuma ku Babulo alendo, amene adzamkupira iye, amene adzataya zonse m’dziko lace, pakuti tsiku la cisauko…

Yeremiya 52

Yerusalemu amangidwa misasa, nalandidwa, napasulidwa 1 Zedekiya anali wa zaka makumi awiri kudza cimodzi pamene analowa ufumu wace; ndipo analamulira m’Yerusalemu zaka khumi kudza cimodzi; dzina la amace ndi Hamutala…

Maliro 1

Tsoka la Yerusalemu 1 Ha! mudziwo unadzala anthu, ukhalatu pa wokha! Ukunga mkazi wamasiye! Waukuruwo mwa amitundu, kalonga wamkazi m’madera a dziko Wasanduka wolamba! 2 Uliralira usiku; misozi yace iri…

Maliro 2

Yerusalemu amangidwa misasa, njala isautsa, mudzi upasuka 1 Ambuye waphimbatu ndi mtambo mwana wamkazi wa Ziyoni, pomkwiyira! Wagwetsa pansi kucokera kumwamba kukoma kwace kwa Israyeli; Osakumbukira poponda mapazi ace tsiku…

Maliro 3

Yeremiya acita nkhawa, adziponya kwa Yehova 1 Ine ndine munthuyu wakuona msauko ndi ndodo ya ukali wace. 2 Wanditsogolera, nandiyendetsa mumdima, si m’kuunika ai. 3 Zoonadi amandibwezera-bwezera dzanja lace monditsutsa…