Eksodo 21
Lamulo la pa kapolo, ndi la pa wakupha mnzace 1 Ndipo awa ndiwo maweruzo amene uziika pamaso pao. 2 Ukagula mnyamata Mhebri, azigwira nchito zaka zisanu ndi cimodzi; koma cacisanu…
Lamulo la pa kapolo, ndi la pa wakupha mnzace 1 Ndipo awa ndiwo maweruzo amene uziika pamaso pao. 2 Ukagula mnyamata Mhebri, azigwira nchito zaka zisanu ndi cimodzi; koma cacisanu…
1 Munthu akaba ng’ombe, kapena nkhosa, nakaipha, kapena kuigulitsa, azilipa ng’ombe zisanu pa ng’ombeyo; ndi nkhosa zinai pa nkhosayo, 2 Akampeza wakuba alimkuboola, nakamkantha kotero kuti wafa, palibe camwazi. 3…
Za mabodza ndi zonyenga 1 Usatola mbiri yopanda pace; usathandizana naye woipa ndi kukhala mboni yocititsa ciwawa. 2 Usatsata unyinji wa anthu kucita coipa; kapena usacita umboni kumlandu, ndi kupatukira…
Mose ndi akuru akwera m’phiri 1 Ndipo iye ananena ndi Mose, Ukwere kudza kwa Yehova, iwe ndi Aroni, Nadabu ndi Abihu, ndi akuru a Israyeli makumi asanu ndi awiri; ndipo…
Zopereka zaufulu zakumanga Malo Opatulika 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Lankhula ndi ana a Israyeli, kuti anditengere copereka; ulandire copereka canga kwa munthu ali yense mtima…
Kacisi ndi nsaru zophimba zace 1 Ndipo uzipanga kacisi ndi nsaru zophimba khumi, za bafuta wa thonje losansitsa, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira; uombemo akerubi, nchito ya mmisiri….
Za guwa la nsembe 1 Ndipo upange guwa la nsembe la mtengo wasitimu, utali wace mikono isanu, ndi kupingasa kwace mikono isanu, guwa la nsembelo likhale lampwamphwa, ndi msinkhu wace…
Za zobvala zopatulika 1 Ndipo akuyandikire Aroni mbale wako, ndi ana ace amuna pamodzi naye, mwa ana a Israyeli, kuti andicitire Ine nchito ya nsembe, ndiwo Aroni, Nadabu, ndi Abihu,…
Mapatulidwe a ansembe 1 Ici ndico uwacitire kuwapatula, andicitire nchito ya nsembe: tenga ng’ombe yamphongo, ndi nkhosa ziwiri zamphongo zangwiro, 2 ndi mkate wopanda cotupitsa, ndi timitanda topanda cotupitsa tosanganiza…
Za guwa la nsembe lofukizapo 1 Ndipo upange guwa la nsembe la kufukizapo; ulipange la mtengo wasitimu. 2 Utali wace ukhale mkono, ndi kupingasa kwace mkono; likhale lampwamphwa; ndi msinkhu…