Yeremiya 36
Mau a Yeremiya alembedwa pampukutu nawerengedwa m’Kacisi, natenthedwa ndi mfumu 1 Ndipo panali caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa…
Mau a Yeremiya alembedwa pampukutu nawerengedwa m’Kacisi, natenthedwa ndi mfumu 1 Ndipo panali caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa…
Yeremiya m’kaidi 1 Ndipo Zedekiya mwana wa Yosiya anakhala mfumu m’malo a Koniya mwana wa Yehoyakimu, amene Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo inamlowetsa mfumu m’dziko la Yuda. 2 Koma ngakhale…
Yeremiya aponyedwa m’dzenje muli thope 1 Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya…
Nebukadirezara alanda Yerusalemu, nalanditsa Yeremiya 1 Caka cacisanu ndi cinai ca Zedekiya mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi, anadza Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo ndi nkhondo yace yonse, ndi kuumangira misasa….
Yeremiya apita kwa Gedaliya ku Mizipa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, Nebuzaradani kapitao wa alonda atammasula pa Rama, pamene anamtenga iye womangidwa m’maunyolo pamodzi ndi am’nsinga…
Gedaliya ndi ena aphedwa ndi Ismayeli 1 Ndipo panali mwezi wacisanu ndi ciwiri, Ismayeli mwana wa Netaniya, mwana wa Elisama, wa mbeu ya mfumu, ndi kapitao wamkuru wa mfumu, ndi…
Yeremiya acenjeza anthu asapite ku Aigupto 1 Ndipo akazembe onse a nkhondo, ndi Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi Jezaniya mwana wace wa Hosiya, ndi anthu onse kuyambira wamng’ono, kufikira…
Amtenga Yeremiya napita naye ku Aigupto 1 Ndipo panali pamene Yeremiya anatha kunena kwa anthu onse mau onse a Yehova Mulungu wao, amene anamtuma iye nao Yehova Mulungu wao, mau…
Acenjeza mowaopsa Ayuda amene adathawira ku Aigupto 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya onena za Ayuda onse amene anakhala m’dziko la Aigupto, okhala pa Migidoli, ndi pa Tapanesi, ndi pa…
Mau a Mulungu kwa Baruki 1 Mau amene ananena Yeremiya mneneri kwa Baruki mwana wace wa Neriya, pamene analemba mau awa m’buku ponena Yeremiya, caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace…