Yeremiya 16
Aneneratu za kutengedwa ukapolo kwa Israyeli ndi kubweranso kwao 1 Ndiponso mau a Mulungu anadza kwa ine, kuti, 2 Usatenge mkazi, usakhale ndi ana amuna ndi akazi m’malo muno. 3…
Aneneratu za kutengedwa ukapolo kwa Israyeli ndi kubweranso kwao 1 Ndiponso mau a Mulungu anadza kwa ine, kuti, 2 Usatenge mkazi, usakhale ndi ana amuna ndi akazi m’malo muno. 3…
Cimo la Yuda ndi losafafanizika 1 Cimo la Yuda lalembedwa ndi peni lacitsulo, ndi nsonga ya diamondi; lalembedwa pa colembapo ca m’mtima mwao, ndi pa nyanga za maguwa a nsembe…
Mbiya ya woumba. Anthu osalapa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2 Tauka, tatsikira ku nyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga. 3 Ndipo ndinatsikira ku…
Nsupa ya woumba isweka, Yerusalemu apasuka 1 Atero Yehova, Pita, nugule nsupa ya woumba, nutenge akuru a anthu, ndi akuru a ansembe; 2 nuturukire ku cigwa ca mwana wace wa…
Pasuri wansembe apanda Yeremiya, nammanga m’kaidi 1 Ndipo Pasuri mwana wace wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkuru m’nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi. 2 Ndipo Pasuri anampanda Yeremiya…
Kufunsira kwa Zedekiya, kuyankha kwa Yeremiya 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa…
1 Yehova atero: Tsikira ku nyumba ya mfumu ya Yuda, ndi kunena komweko mau awa, 2 ndi kuti, Tamvani mau a Yehova, Inu mfumu ya Yuda, amene mukhala pa mpando…
Mau akutsutsa abusa osakhulupirika 1 Tsoka abusa amene athetsa nabalalitsa nkhosa za busa langa! ati Yehova. 2 Cifukwa cace atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, ponenera abusa amene adyetsa anthu anga:…
Za mitanga iwiri ya nkhuyu; za mtundu wao m’tsogolo 1 Yehova anandionetsa ine, ndipo, taonani, mitanga iwiri ya nkhuyu yoikidwa pakhomo pa Kacisi wa Yehova; Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo…
Atalangidwa Aisrayeli adzalangidwa amitundu ena omwe 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya za anthu onse a Yuda caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda; ndico caka…