Yeremiya 6
Acenjezedwa kuti adani adzamangira Yerusalemu misasa 1 Ananu a Benjamini, pulumukani pothawa pakati pa Yerusalemu, ombani lipenga m’Tekoa, kwezani cizindikiro m’Beti-hakeremu; pakuti caoneka coipa coturuka m’mpoto ndi kuononga kwakukulu. 2…