Yesaya 52

1 Galamuka galamuka, tabvala mphamvu zako, Ziyoni; tabvala zobvala zako zokongola, Yerusalemu, mzinda wopatulika; pakuti kuyambira tsopano sadzalowanso kwa iwe wosadulidwa ndi wodetsedwa. 2 Dzisanse pfumbi; uka, khala tsonga, Yerusalemu;…

Yesaya 53

Masomphenya a cisauko ndi ulemerero wa Mtumiki wa Yehova 1 Ndani wamvera uthenga wathu? Ndi mkono wa Yehova wabvumbulukira yani? 2 Pakuti ameneyo adzaphuka pamaso pace ngati mtengo wanthete, ndi…

Yesaya 54

Zokoma zimene Yehova adzacitira Mpingo wao 1 Yimba, iwe wouma, amene sunabala; yimba zolimba ndi kupfuula zolimba, iwe amene sunabala mwana; pakuti ana a mfedwa acuruka koposa ana a mkazi…

Yesaya 55

Osauka onse aitanidwa alandire cipulumutso 1 Inu nonse, inu akumva ludzu, idzani kumadzi; ndi osowa ndarama idzani inu mugule mudye; inde idzani, mugule vinyo ndi mkaka opanda ndarama ndi opanda…

Yesaya 56

Malonjezo a kwa iwo osunga Sabata 1 Atero Yehova, Sungani inu ciweruziro, ndi kucita cilungamo; pakuti cipulumutso canga ciri pafupi kudza, ndi cilungamo canga ciri pafupi kuti cib zumbulutsidwe, 2…

Yesaya 57

Kupembedza mafano kwa Israyeli 1 Wolungama atayika, ndipo palibe munthu wosamalirapo; ndipo anthu acifundo atengedwa, palibe wolingalira kuti wolungama acotsedwa pa coipa cirinkudza. 2 Iye alowa mumtendere, iwo apuma pa…

Yesaya 58

Kusala kosayenera, ndi kusala koyenera 1 Pfuula zolimba, usalekerere, kweza mau ako ngati lipenga, ndi kuwafotokozera anthu anga colakwa cao, ndi banja la Yakobo macimo ao. 2 Koma iwo andifuna…

Yesaya 59

Aulula zoipa za mtundu wao 1 Taonani, mkono wa Yehova sufupika, kuti sungathe kupulumutsa; khutu lace siliri logontha, kuti silingamve; 2 koma zoipa zanu zakulekanitsani inu ndi Mulungu wanu; ndipo…

Yesaya 60

Ulemerero wa Yerusalemu ubwezedwa 1 Nyamuka, wala, pakuti kuunika kwake kwafika, ndi ulemerero wa Yehova wakuturukira. 2 Pakuti taona, mdima udzaphimba dziko lapansi, ndi mdima wa bii mitundu ya anthu;…

Yesaya 61

Alalikira Uthenga Wabwino wa cipulumutso 1 Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am’nsinga…