Yesaya 42
Mtumiki wa Yehova 1 Taona Mtumiki wanga, amene ndimgwiriziza; Wosankhika wanga, amene moyo wanga ukondwera naye; ndaika mzimu wanga pa Iye; Iye adzaturutsira amitundu ciweruziro. 2 Iye sadzapfuula, ngakhale kukuwa,…
Mtumiki wa Yehova 1 Taona Mtumiki wanga, amene ndimgwiriziza; Wosankhika wanga, amene moyo wanga ukondwera naye; ndaika mzimu wanga pa Iye; Iye adzaturutsira amitundu ciweruziro. 2 Iye sadzapfuula, ngakhale kukuwa,…
Mulungu Yehova yekha apulumutsa Israyeli 1 Koma tsopano atero Yehova, amene anakulenga iwe Yakobo, ndi Iye amene anakupanga iwe Israyeli, Usaope, cifukwa ndakuombola iwe, ndakuchula dzina lako, iwe uli wanga….
Mulungu ndi wamkulukulu, mafano ndi acabe 1 Koma tsopano, imva Yakobo, mtumiki wanga, ndi Israyeli, amene ndakusankha; 2 atero Yehova, amene anakutenga iwe, nakuumba kucokera m’mimba, amene adzathangata iwe. Usaope…
Yehova amuyesa Koresi cipangizo cace 1 Atero Yehova kwa wodzozedwa wace kwa Koresi, amene dzanja lace lamanja ndaligwiritsa, kuti agonjetse mitundu ya anthu pamaso pace, ndipo ndidzamasula m’cuuno mwa mafumu;…
Aneneratu za kupasuka kwa mafano a ku Babulo 1 Beli agwada pansi, Nebo awerama; mafano ao ali pa zoweta, ndi pa ng’ombe; zinthu zimene inu munanyamula ponseponse ziyesedwa mtolo, katundu…
Babulo adzaonongeka konse 1 Tsika, ukhale m’pfumbi, namwaliwe, mwana wamkazi wa Babulo; khala pansi popanda mpando wacifumu, mwana wamkazi wa Akasidi, pakuti iwe sudzayesedwanso wozizira ndi wololopoka. 2 Tenga mipero,…
Awadandaulira Aisrayeli, awacenteza, nalonjezana nao 1 Imvani inu ici, banja la Yakobo, amene muchedwa ndi dzina la Israyeli, amene munaturuka m’madzi a Yuda amene mulumbira dzina la Yehova ndi kuchula…
Mtumiki wa Yehova, kuunika kwa amitundu 1 Mverani Ine, zisumbu inu, mumvere anthu inu akutari; Yehova anandiitana Ine ndisanabadwe; m’mimba mwa amai Iye anachula dzina langa; 2 nacititsa pakamwa panga…
Mtumiki wa Yehova anyozedwa koma athandizidwa 1 Atero Yehova, Kalata wa cilekaniro ca amako ali kuti amene ndinamsudzula naye? pena ndani wa angongole anga amene ndamgulitsa iwe? Taona cifukwa ca…
Israyeli akonzedwanso napulumutsidwa 1 Mverani Ine, inu amene mutsata cilungamo, inu amene mufuna Yehova; yang’anani ikuthanthwe, kumene inu munasemedwamo, ndi kuuna kwa dzenje, kumene inu munakumbidwamo. 2 Yang’anani kwa Abrahamu…