Yesaya 32

Ufumu wa mfumu yolungama 1 Taonani mfumu idzalamulira m’cilungamo, ndi akalonga adzalamulira m’ciweruzo. 2 Ndipo munthu adzakhala monga pobisalira mphepo, ndi pousira cimphepo; monga mitsinje yamadzi m’malo ouma, monga mthunzi…

Yesaya 33

Adani a anthu a Mulungu adzapasuka; Yerusalemu adzabwezedwa ulemu 1 Tsoka kwa iwe amene usakaza, cinkana sunasakazidwa; nupangira ciwembu, cinkana sanakupangira iwe ciwembu! Utatha kusakaza, iwe udzasakazidwa; ndipo utatha kupangira…

Yesaya 34

Yehova aipidwa ndi amitundu 1 Idzani pafupi, amitundu inu, kuti mumve; mverani anthu inu, dziko limve, ndi za mommo; dziko ndi zinthu zonse zoturukamo. 2 Pakuti Yehova akwiyira amitundu onse,…

Yesaya 35

Cikondwerero ca Ziyoni m’tsogolomo 1 Cipululu ndi malo ouma adzakondwa; ndipo dziko loti se lidzasangalala ndi kuphuka ngati duwa. 2 Lidzaphuka mocuruka ndi kusangalala, ngakhale kukondwa ndi kuyimba; lidzapatsidwa ulemerero…

Yesaya 36

Nkhondo ya Sanakeribu idzera Yerusalemu 1 Koma panali caka cakhumi ndi cinai ca mfumu Hezekiya, Sanakeribu, mfumu ya Asuri anadza, nathira nkhondo pa midzi ya malinga yonse ya Yuda, nailanda….

Yesaya 37

Mwa mantha Hezekiya aitana mnenert Yesaya 1 Ndipo panali pamene mfumu Hezekiya anamva, anang’amba zobvala zace, nabvala ciguduli, nalowa m’nyumba ya Yehova. 2 Ndipo anatumiza Eliakimu, wapanyumba, ndi Sebina, mlembi,…

Yesaya 38

Kudwala kwa Hezekiya ndi kuciritsidwa kwace 1 Masiku amenewo Hezekiya anadwala, nafuna kufa. Ndipo Yesaya mneneri, mwana wa Amozi, anadza kwa iye, nati kwa iye, Atero Yehova, Konza nyumba yako,…

Yesaya 39

Hezekiya aonetsa amithenga a ku Babulo cuma cace, Yesaya namdzudzula 1 Nthawi imeneyo Merodakibaladani, mwana wa Baladani, mfumu ya ku Babulo, anatumiza akalata ndi mphatso kwa Hezekiya; pakuti anamva kuti…

Yesaya 40

Lonjezo la cipulumutso ca Israyeli 1 Mutonthoze, mutonthoze mtima wa anthu anga, ati Mulungu wanu. 2 Munene inu zotonthoza mtima kwa Yerusalemu, nimupfuulire kwa iye, kuti nkhondo yace yatha, kuti…

Yesaya 41

Yehova yekha ndiye Mulungu, lsrayeli amkhulupirire Iye yekha yekha 1 Khalani cete pamaso pa Ine, zisumbu inu, anthu atengenso mphamvu; ayandikire; pamenepo alankhule; tiyeni, tiyandikire pamodzi kuciweruziro. 2 Ndani anautsa…