Yesaya 22
Aneneratu za kumangidwa misasa Yerusalemu 1 Katundu wa cigwa ca masomphenya. Mwatani kuti mwakwera nonsenu pamacindwi? 2 Iwe amene wadzala ndi zimpfuu, mudzi waphokoso, mudzi wokondwa; ophedwa ako, sanaphedwa ndi…
Aneneratu za kumangidwa misasa Yerusalemu 1 Katundu wa cigwa ca masomphenya. Mwatani kuti mwakwera nonsenu pamacindwi? 2 Iwe amene wadzala ndi zimpfuu, mudzi waphokoso, mudzi wokondwa; ophedwa ako, sanaphedwa ndi…
Kupasuka ndi kumangidwanso kwa Turo 1 Katundu wa Turo. Kuwani, inu ngalawa za Tarisi; cifukwa wapasudwa, kulibenso nyumba, kulibe polowera; kucokera ku dziko la Kitimo kwabvumbulutsidwa kwa iwo. 2 Khalani…
Cilango ca Mulungu ca pa dziko la Israyeli, ndi pa dziko lonse lapansi 1 Taonani, Yehova apululutsa dziko, nalipasula, nalitembenuza dodolido, nabalalitsa okhalamo ace. 2 Ndipo padzakhala monga ndi anthu,…
Nvimbo yakulemekeza cifundo ca Mulungu 1 Yehova, Inu ndinu Mulungu wanga, ndidzakukuzani Inu, ndidzatamanda dzina lanu, cifukwa mwacita zinthu zodabwitsa, ngakhale: zauphungu zakale, mokhulupirika ndi m’zoonadi. 2 Cifukwa Inu mwasandutsa…
Nyimbo yakulemekeza kuciniiriza kwa Yehova 1 Tsiku limenelo adzayimba nyimbo imeneyi m’dziko la Yuda, Ife tiri ndi mudzi wolimba; Iye adzaikacipulumutso cikhale macemba ndi malinga. 2 Tsegulani pazipata, kuti mtundu…
Munda wamphesa wa Yehova 1 Tsiku limenelo Yehova ndi lupanga lace lolimba ndi lalikuru ndi lamphamvu adzalanga nangumi njoka yotamanga, ndi nangumi njoka yopindika-pindika; nadzapha cing’ona cimene ciri m’nyanja. 2…
Kulangidwa kwa Efraimu ndi Yuda cifukwa ca kuuma mtima kwao 1 Tsoka kwa korona wakunyada wa oledzera a Efraimu, ndi kwa duwa lakufota la ulemerero wace wokongola, limene liri pamutu…
Aneneratu za kulangidwa kwa Yuda wosakhulupirika, komanso za cipulumutso cace 1 Eya Arieli, Arieli, mudzi umene Davide anamangapo zithando! oniezerani caka ndi caka; maphwando afikenso; 2 pamenepo ndidzasautsa Arieli, ndipo…
1 Tsoka okhulupirira Aigupto. Tsoka kwa ana opanduka, ati Yehova, amene atenga uphungu koma si pa Ine; napangana pangano opanda mzimu wanga, kuti aonjezere cimo ndi cimo; 2 amene ayenda…
Toka otama cithandizo ca Aigupto 1 Tsoka kwa iwo amene atsikira kunka ku Aigupto kukathandizidwa, natama akavalo; nakhulupirira magareta, pakuti ali ambiri, ndi okwera pa akavalo, pakuti ali a mphamvu…