Yesaya 12

Ciyamiko ca anthu a Mulungu atalangidwa 1 Tsiku lomwelo udzati, Ndikuyamikani inu Yehova; pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu wacoka, ndipo mutonthoza mtima wanga. 2 Taonani, Mulungu ndiye cipulumutso canga; ndidzakhulupira,…

Yesaya 13

Aneneratu za kutyoka kwa ufumu wa Babulo, ndi kubweza Israyeli kwao 1 Katundu wa Babulo, imene anaiona Yesaya mwana wa Amozi. 2 Kwezani mbendera pa phiri loti se, kwezani mau…

Yesaya 14

1 Pakuti Ambuye adzamcitira cifundo Yakobo, ndipo adzasankhanso Israyeli, ndi kuwakhazikitsa m’dziko la kwao; ndipo acilendo adzadziphatika okha kwa iwo, nadzadzigumikiza ku nyumba ya Yakobo. 2 Ndipo mitundu ya anthu…

Yesaya 15

Aneneratu za kuonongeka kwa Moabu 1 Katundu wa Moabu. Pakuti usiku umodzi Ara wa ku Moabu wapasuka, nakhala cabe; usiku umodzi Kiri wa Moabu wapasuka, nakhala cabe. 2 Akwera kukacisi,…

Yesaya 16

1 Tumizani inu ana a nkhosa kwa wolamulira wa dziko kucokera ku Sela kunka kucipululu, mpaka ku phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni. 2 Pakuti ana akazi a Moabu adzakhala…

Yesaya 17

Aneneratu za Damasiko ndi Efraimu 1 Katundu wa Damasiko. Taonani, Damasiko wacotsedwa usakhalenso mudzi, ndimo udzangokhala muunda wopasudwa. 2 Midzi ya Aroeri yasiyidwa; idzakhala ya zoweta zogona pansi, opanda woziopsya….

Yesaya 18

Aneneratu za Etiopia 1 Ha, dziko lakukupuza mapiko, liri tsidya lija la nyanja za Etiopia; 2 limene litumiza mithenga panyanja m’ngalawa zatnabungwa zoyenda m’madzi, ndi kuti, Mukani, inu mithenga yoyenda…

Yesaya 19

Aneneratu za Aigupto 1 Katundu wa Aigupto. Taonani, Yehova wakwera pamwamba pa mtambo wothamanga, nadza ku Aigupto; ndi mafano a Aigupto adzagwedezeka pakufika kwace, ndi mtima wa Aigupto udzasungunuka pakati…

Yesaya 20

Cizindikilo cakutyoka Aigupto ndi Etiopia 1 Caka cimene kazembe wa ku Asuri anafika ku Asidodi, muja Sarigoni mfumu ya Asuri anamtumiza iye, ndipo iye anamenyana ndi Asidodi, naugonjetsa. 2 Nthawi…

Yesaya 21

Aneneratu za kugwa kwa Babulo 1 Katundu wa cipululu ca kunyanja. Monga akabvumvulu a kumwela apitirira, kufumira kucipululu ku dziko loopsya. 2 Masomphenya obvuta aonetsedwa kwa ine; wogula malonda wonyenga…