Eksodo 11

Cozizwitsa cakhumi: Imfa ya ana oyamba kubadwa 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Watsala moo umodzi ndidzamtengera Farao, ndi Aigupto; pambuyo pace adzakulolani mucoke kuno; pamene akulolani kupita, zoonadi adzakuingitsani…

Eksodo 12

Kuikidwa kwa Paskha 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2 Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa caka….

Eksodo 13

Ana ovamba kubadwa apatulidwira Yehova 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi kuti, 2 Ndipatulire Ine yense woyamba kubadwa, wotsegulira pa amace mwa ana a Israyeli, mwa anthu ndi mwa…

Eksodo 14

Farao alondola Aisrayeli 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Lankhula ndi anthu a Israyeli kuti abwerere m’mbuyo nagone patsogolo pa Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja yamcere,…

Eksodo 15

1 Nyimbo yolemekeza Mulungu, Pamenepo Mose ndi ana a Israyeli anayimbira Yehova nyimbo iyi, nanena, ndi kuti, Ndidzayimbira Yehova pakuti wapambanatu; Kavalo ndi wokwera wace anawaponya m’nyanja. 2 Yehova ndiye…

Eksodo 16

Zinziri ndi mana 1 Ndipo anacoka ku Elimu, ndi khamu lonse la ana a Israyeli linalowa m’cipululu ca Sini, ndico pakati pa Elimu ndi Sinai, tsiku lakhumi ndi cisanu la…

Eksodo 17

Madzi aturuka m’thanthwe ku Horebe 1 Ndipo khamu lonse la ana a Israyeli linacoka m’cipululu ca Sini, m’zigono zao, monga mwa mau a Yehova, nagona m’Refidimu. Koma kumeneko kunalibe madzi…

Eksodo 18

Yetero azonda Mose nampangira 1 Ndipo Yetero, wansembe wa Midyani, mpongozi wa Mose, anamva zonse zimene Mulungu adacitira Mose ndi Israyeli anthu ace, kuti Yehova adaturutsa Israyeli m’Aigupto. 2 Ndipo…

Eksodo 19

Mulungu alamulira anthu za ku Sinai 1 Mwezi wacitatu ataturuka ana a Israyeli m’dziko la Aigupto, tsiku lomwelo, analowa m’cipululu ca Sinai. 2 Pakuti anacoka ku Refidimu, nalowa m’cipululu ca…

Eksodo 20

Malamulo khumi a Mulungu 1 Ndipo Mulungu ananena mau onse amenewa, nati: 2 INE ndine YEHOVA Mulungu wako, amene ndinaturutsa iwe ku dziko la Aigupto, ku nyumba ya akapolo. 3…