Miyambi 13
1 Mwana wanzeru amamvera mwambo wa atate; Koma wonyoza samvera cidzudzulo. 2 Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m’kamwa mwace; Koma moyo wa aciwembu udzadya ciwawa. 3 Wogwira pakamwa pace…
1 Mwana wanzeru amamvera mwambo wa atate; Koma wonyoza samvera cidzudzulo. 2 Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m’kamwa mwace; Koma moyo wa aciwembu udzadya ciwawa. 3 Wogwira pakamwa pace…
1 Mkazi yense wanzeru amanga banja lace; Koma wopusa alipasula ndi manja ace. 2 Woyenda moongoka mtima aopa Yehova; Koma wokhota m’njira yace amnyoza, 3 M’kamwa mwa citsiru muli ntyole…
1 Mayankhidwe ofatsa abweza mkwiyo; Koma mau owawitsa aputa msunamo. 2 Lilime la anzeru linena bwino zomwe adziwa; Koma m’kamwa mwa opusa mutsanulira utsiru. 3 Maso a Yehova ali ponseponse,…
1 Malongosoledwe a mtima nga munthu; Koma mayankhidwe a lilime acokera kwa Yehova. 2 Njira zonse za munthu ziyera pamaso pace; Koma Yehova ayesa mizimu. 3 Pereka zocita zako kwa…
1 Nyenyeswa youma, pokhala mtendere, Iposa nyumba yodzala nyama yansembe, pali makangano. 2 Kapolo wocitamwanzeru Adzalamulira mwana wocititsa manyazi, Nadzagawana nao abale colowa. 3 Siliva ali ndi mbiya yosungunulira, golidi…
1 Wopanduka afunafuna niro cace, Nakangana ndi nzeru yonse yeniyeni. 2 Wopusa sakondwera ndi kuzindikira; Koma kungobvumbulutsa za m’mtima mwace. 3 Pakudza wamphulupulu padzanso kunyoza; Manyazi natsagana ndi citonzo. 4…
1 Wosauka woyenda mwangwiro Aposa wokhetsa milomo ndi wopusa. 2 Kukhumba kosadziwa sikuli kwabwino; Ndipo wofulumira ndi mapazi ace amacimwa. 3 Utsiru wa munthu ukhotetsa njira yace; Mtima wace udandaula…
1 Vinyo acita ciphwete, cakumwa caukali cisokosa; Wosocera nazo alibe nzeru. 2 Kuopsya kwa mfumu ndiko kubangula kwa mkango; Womputa acimwira moyo wace wace. 3 Kuli ulemu kwa mwamuna kupewa…
1 Mtima wa mfumu uli m’dzanja la Yehova ngati mitsinje ya madzi; Aulozetsa komwe afuna. 2 Njira zonse za munthu zilungama pamaso pace; Koma Yehova ayesa mitima. 3 Kucita cilungamo…
1 Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri; Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi. 2 Wolemera ndi wosauka akumana, Wolenga onsewo ndiye Yehova. 3 Wocenjera aona zoipa, nabisala; Koma acibwana…