Miyambi 3

Malangizo a kuopa, kukhulupira, ndi kumvera Yehova 1 Mwananga, usaiwale malamulo anga, Mtima wako usunge malangizo anga; 2 Pakuti adzakuonjezera masiku ambiri, Ndi zaka za moyo ndi mtendere. 3 Cifundo…

Miyambi 4

Ceniezo lakuti afune Nzeru nalewe njira za oipa 1 Ananu, mverani mwambo wa atate, Nimuchere makutu mukadziwe luntha; 2 Pakuti ndikuphunzitsani zabwino; Musasiye cilangizo canga. 3 Pakuti ndinali mwana kwa…

Miyambi 5

Acenjere naye mkazi woipa 1 Mwananga, mvera nzeru yanga; Cherera makutu ku luntha langa; 2 Ukasunge zolingalira, Milomo yako ilabadire zomwe udziwa. 3 Pakuti milomo ya mkazi waciwerewere ikukha uci;…

Miyambi 6

Za kuperekera mnzace cikole. Zisanu ndi ziwiri zoipira Mulungu 1 Mwananga, ngati waperekera mnzako cikole, Ngati wapangana kulipirira mlendo, 2 Wakodwa ndi mau a m’kamwa mwako, Wagwidwa ndi mau a…

Miyambi 7

Acenjere naye mkazi woipa 1 Mwananga, sunga mau anga, Ukundike malangizo anga; 2 Sunga malangizo anga, nukhale ndi moyo; Ndi malamulo anga ngati mwana wa diso lako. 3 Uwamange pa…

Miyambi 8

Nzeru ipambana m’kucita kwace 1 Kodi nzeru siitana, Luntha ndi kukweza mau ace? 2 Iima pamwamba pa mtunda, Pa mphambano za makwalala; 3 Pambali pa cipata polowera m’mudzi, Polowa anthu…

Miyambi 9

Madyerero a Nzeru 1 Nzeru yamanga nyumba yace, Yasema zoimiritsa zace zisanu ndi ziwiri; 2 Yaphera nyama yace, nisanganiza vinyo wace, Nilongosolanso pa gome lace. 3 Yatuma anamwali ace, iitana…

Miyambi 10

Miyambo yosiyana-siyana; Miyambo ya Sotomo 1 Mwana wanzeru akondweretsa atate; Koma mwana wopusa amvetsa amace cisoni. 2 Cuma ca ucimo sicithangata: Koma cilungamo cipulumutsa kuimfa. 3 Yehova samvetsa njala moyo…

Miyambi 11

1 Muyeso wonyenga unyansa Yehova; Koma mulingo wamphumphu umsekeretsa. 2 Pakudza kudzikuza padzanso manyazi; Koma nzeru iri ndi odzicepetsa, 3 Kuongoka mtima kwa olungama kuwatsogolera; Koma kukhota kwa aciwembu kudzawaononga….

Miyambi 12

1 Wokonda mwambo akonda kudziwa; Koma wakuda cidzudzulo apulukira. 2 Yehova akomera mtima munthu wabwino; Koma munthu wa ziwembu amtsutsa, 3 Munthu sadzakhazikika ndi udio, Muzu wa olungama sudzasunthidwa. 4…