Masalmo 143

Davide apempha Mulungu amlanditse msanga kwa adani ace Salmo la Davide. 1 Imvani pemphero langa, Yehova; ndicherere khutu kupemba kwanga; Ndiyankheni mwa cikhulupiriko canu, mwa cilungamo canu. 2 Ndipo musaitane…

Masalmo 144

Davide ayamika Mulungu kuti anamcinjiriza, napempha ampulumutse kuti anthu adalenso Salmo la Davide. 1 Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, Wakuphunzitsa manja anga acite nkhondo, Zala zanga zigwirane nao: 2 Ndiye cifundo…

Masalmo 145

Ukuru ndi ukoma wa Mulungu Salmo lolemekeza; la Davide, 1 Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu; Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi. 2 Masiku onse ndidzakuyamikani; Ndi kulemekeza dzina lanu…

Masalmo 146

Cifoko ca munthu, cikhulupiriko ca Mulungu 1 Haleluya; Ulemekeze Yehova, moyo wanga, 2 Ndidzalemekeza Yehovam’moyo mwanga; Ndidzayimbira zomlemekeza Mulungu wanga pokhala ndi moyo ine. 3 Musamakhulupirira zinduna, Kapena mwana wa…

Masalmo 147

Alemekeze dzina la Mulungu cifukwa ca zokoma amacitira anthu ace 1 Haleluya; Pakuti kuyimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; Pakuti cikondwetsa ici, cilemekezo ciyenera. 2 Yehova amanga Yerusalemu; Asokolotsa otayika a…

Masalmo 148

Zolengedwa zonse zilemekeze Mulungu 1 Haleluya. Lemekezani Yehova kocokera kumwamba; Mlemekezeni m’misanje. 2 Mlemekezeni, angelo ace onse; Mlemekezeni, makamu ace onse. 3 Mlemekezeni, dzuwa ndi mwezi; Mlemekezeni, nyenyezi zonse zaunikira….

Masalmo 149

Okhulupirira onse alemekeze Mulungu wao 1 Haleluya, Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano, Ndi cilemekezo cace mu msonkhano wa okondedwa ace. 2 Akondwere Israyeli mwa Iye amene anamlenga; Ana a Ziyoni asekere…

Masalmo 150

Zolengedwa zonse zilemekeze Mulungu 1 Haleluya, Lemekezani Mulungu m’malo ace oyera; Mlemekezeni m’thambo la mphamvu yace. 2 Mlemekezeni cifukwa ca nchito zace zolimba; Mlemekezeni monga mwa ukulu wace waunjinji. 3…

Miyambi 1

Zocitira miyambi 1 MIYAMBI ya Solomo mwana wa Davide, mfumu ya Israyeli. 2 Kudziwa nzeru ndi mwambo; Kuzindikira mau ozindikiritsa; 3 Kulandira mwambo wakusamalira macitidwe, Cilungamo, ciweruzo ndi zolunjika; 4…

Miyambi 2

Ukoma ndi phindu tace la Nzeru 1 Mwananga, ukalandira mau anga, Ndi kusunga malamulo anga; 2 Kucherera makutu ako kunzeru, Kulozetsa mtima wako kukuzindikira; 3 Ukaitananso luntha, Ndi kupfuulira kuti…