Masalmo 133
Cikondano ca abale ndi cokoma Nyimbo yokwerera; ya Davide. 1 Onani, nkokoma ndi kokondweretsa ndithu Kuti abale akhale pamodzi! 2 Ndiko ngati mafuta a mtengo wace pamutu, Akutsikira ku ndebvu,…
Cikondano ca abale ndi cokoma Nyimbo yokwerera; ya Davide. 1 Onani, nkokoma ndi kokondweretsa ndithu Kuti abale akhale pamodzi! 2 Ndiko ngati mafuta a mtengo wace pamutu, Akutsikira ku ndebvu,…
Afulumizidwa anthu kulemekeza Yehova Nyimbo vokwerera, 1 Taonani, lemekezani Yehova, atumiki a Yehova inu nonse, Akuimirira m’nyumba ya Yehova usiku, 2 Kwezani manja anu ku malo oyera, Nimulemekeze Yehova. 3…
Mulungu alemekezedwa pa ukulu wace. Mafano ndi acabe 1 Haleluya; Lemekezani dzina la Yehova; Lemekezani inu atumiki a Yehova: 2 Inu akuimirira m’nyumba ya Yehova, M’mabwalo a nyumba ya Mulungu…
Mulungu alemekezedwe pa cifundo cace 1 Yamikani Yehova pakuti ndiye wabwino: Pakuti cifundo cace ncosatha. 2 Yamikani Mulungu wa milungu: Pakuti cifundo cace ncosatha. 3 Yamikani Mbuye wa ambuye: Pakuti…
Kudandaula kwa Ayuda ku Babulo 1 Ku mitsinje ya ku Babulo, Kumeneko tinakhala pansi, inde tinalira, Pokumbukila Ziyoni. 2 Pa msondodzi uli m’mwemo Tinapacika mazeze athu. 3 Popeza pamenepo akutigwirawo…
Davide ayamika Mulungu pa kukhulupirika kwace, naneneratu kuti mafumu onse adzatero Salmo la Davide. 1 Ndidzakuyamikani ndi mtima wangawonse; Ndidzayimba zakukulemekezani patsogolo pa milungu, 2 Ndidzagwadira kuloza ku Kacisi wanu…
Mulungu ali ponse ponse, adziwa zonse Kwa Mkulu wa Nsembe. Salmo la Davide. 1 Munandisanthula, Yehova, nimundidziwa. 2 Inumudziwakukhalakwangandi kuuka kwanga, Muzindikira lingaliro langa muli kutali. 3 Muyesa popita ine…
Davide apempha Mulungu amlanditse kwa mdani woipa wamphamvu Kwa Mkulu wa nsembe; Salmo la Davide. 1 Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; Ndisungeni kwa munthu waciwawa; 2 Amene adzipanga zoipa mumtima…
Davide apempha Mulungu amthandize poyesedwa ndi zoipa Salmo la Davide. 1 Yehova, ndaitana kwa Inu; ndifulumireni ine; Mundicherere khutu, pamene ndiitana kwa Inu. 2 Pempherolanga liikike ngaticofukiza pamaso panu; Kukweza…
Pemphero pakuopsedwa kwakukuru Cilangizo ca Davide, muja anakhala m’phanga; Pemphero, 1 Ndipfuula nalo liu langa kwa Yehova; Ndi mau anga ndipemba kwa Yehova. 2 Nditsanulirakudandaulakwanga pamaso pace; Ndionetsa msauko wanga…