Eksodo 1

Masautso a ana a Israyeli m’Aigupto 1 NDIPO maina a ana a Israyeli, amene analowa m’Aigupto ndi Yakobo ndi awa, analowa munthu ndi banja lace: 2 Rubeni, Simeoni, Levi ndi…

Eksodo 2

Kubadwa kwa Mose 1 Ndipo anamuka munthu wa banja la Levi, natenga mwana wamkazi wa Levi. 2 Ndipo anaima mkaziyo, naonamwanawamwamuna; m’mene anamuona kuti ali wokoma, anambisa miyezi itatu. 3…

Eksodo 3

1 Koma Mose analikuweta gulu la Yetero mpongozi wace, wansembe wa ku Midyani; natsogolera gululo m’tsogolo mwa cipululu, nafika ku phiri la Mulungu, ku Horebe. 2 Ndipo mthenga wa Molungu…

Eksodo 4

Mose alandira mphamvu yakucita zodabwiza 1 Ndipo Mose anayankha nati, Koma taonani, sadzakhulupirira ine, kapena kumvera mau anga; pakuti adzanena, Yehova sanakuonekera iwe. 2 Ndipo Yehova ananena naye, Ico nciani…

Eksodo 5

Kupempha kwa Mose ndi Aroni kuipsa mlandu wa Aisrayeli 1 Ndipo pambuyo pace Mose ndi Aroni analowa nanena ndi Farao, Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, Lola anthu anga apite, kundicitira…

Eksodo 6

1 Ndipo Yehova ananena kwa Mose, Tsopano udzaona comwe ndidzacitira Farao; pakuti ndi dzanja lamphamvu adzawalola apite, inde ndi dzanja lamphamvu adzawaingitsa m’dziko lace. 2 Ndipo Mulungu ananena ndi Mose,…

Eksodo 7

1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Taona, ndakuika ngati Mulungu kwa Farao; ndi Aroni mkuru wako adzakhala mneneri wako. 2 Iwe uzdankhula zonse ndikulamulira; ndi Aroni mkuru wako azilankhula kwa…

Eksodo 8

Cozizwitsa caciwiri: Acule 1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, nunene naye, Atero Yehova, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire. 2 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda…

Eksodo 9

Cozizwitsa cacisanu: Kalira pa zoweta 1 Pamenepo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, numuuze, Atero Yehova Mulungu wa Ahebri, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire. 2 Pakuti ukakana kuwalola…

Eksodo 10

Cozizwitsa ca 8: D’zombe 1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao; pakuti ndaumitsa mtima wace, ndi mtima wa anyamata ace, kuti ndiike zizindikilo zanga izi pakati pao; 2…