Masalmo 103

Alemekeze Yehovapa cifundo cace cacikuru Salmo la Da vide. 1 Lemekeza Yehova, moyo wanga; Ndi zonse za m’kati mwanga zilemekeze dzina lace loyera. 2 Lemekeza Yehova, moyo wanga, Ndi kusaiwala…

Masalmo 104

Ulemerero wa Mulungu m’zolengedwa ndi m’kuzisunga komwe 1 Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkurukuru; 2 Mubvala ulemu ndi cifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi cobvala;…

Masalmo 105

Alemekeza Yehova pa zodabwiza adazicitira ana a Israyeli 1 Yamikani Yehova, itanirani pa dzina lace; Bukitsani mwa mitundu ya anthu zocita Iye. 2 Myimbireni, myimbireni zomlemekeza; Fotokozerani zodabwiza zace zonse….

Masalmo 106

Israyeli anapikisana ndi Yehova kwambiri, Iye nawalanga nawalanditsanso Amlemekezepo 1 Haleluya. Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino: Pakuti cifundo cace ncosatha. 2 Adzafotokoza ndani nchito zamphamvu za Yehova, Adzamveketsa ndani…

Masalmo 107

Olanditsidwa, alendo, omangidwa, odwala, amarinyero ndi onse ena alemekeze Yehova 1 Yamikani Yehova pakuti Iye ndiye wabwino; Pakuti cifundo cace ncosatha. 2 Atere oomboledwa a Yehova, Amene anawaombola m’dzanja la…

Masalmo 108

Davide ayimbira Mulungu womgonjetsera adani Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Wakhazikika mtima wanga, Mulungu; Ndidzayimba, inde ndidzayimba zolemekeza, ndiko ulemerero wanga. 2 Galamukani, cisakasa ndi zeze; Ndidzauka ndekha mamawa. 3…

Masalmo 109

Davide apempha Mulungu alange oipa, amlanditse m’manja mwao Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salmo la Davide, 1 Mulungu wa cilemekezo canga, musakhale cete; 2 Pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa…

Masalmo 110

Ufumu wa Ambuye Salmo la Davide, 1 Yehova ananena kwa Ambuye wanga, Khalani pa dzanja lamanja langa, Kufikira nditaika adani anu copondapo mapazi anu. 2 Yehova adzatumiza ndodo ya mphamvu…

Masalmo 111

Alemekeza Mulungu pa nchito zao zazikuru zokoma 1 Haleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, Mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano. 2 Nchito za Yehova nzazikuru, Zofunika ndi onse akukondwera…

Masalmo 112

Adalitsidwa akuopa Mulungu 1 Haleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, Wakukondwera kwambiri ndi malamulo ace, 2 Mbeu yace idzakhala yamphamvu pa dziko lapansi; Mbadwo wa oongoka mtima udzadalitsidwa. 3 M’nyumba mwace…