Masalmo 93

Ufumu wa Mulungu ndiwo wa ulemerero, mphamvu, ndi ciyero 1 Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu; Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m’cuuno; Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka. 2 Mpando wacifumu…

Masalmo 94

Mulungu wolungama adzaweruza otpa 1 Mulungu wakubwezera cilango, Yehova, Mulungu wakubwezera cilango, muoneke wowala. 2 Nyamukani, Inu woweruza wa dziko lapansi: Bwezerani odzikuza coyenera iwo. 3 Oipa adzatumpha ndi cimwemwe…

Masalmo 95

Adandaulira anthu alemekeze namvere Mulungu wao wamkuru 1 Tiyeni tiyimbire Yehova mokondwera; Tipfuule kwa thanthwe la cipulumutso cathu. 2 Tidze naco ciyamiko pamaso pace, Timpfuulire Iye mokondwera ndi masalmo. 3…

Masalmo 96

Onse a pansi pano ndi am’mwamba omwe alemekeze Mulungu 1 Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano; Myimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi. 2 Myimbireni Yehova, lemekezani dzina lace; Lalikirani cipulumutso cace tsiku…

Masalmo 97

Ulemerero wa ufumu wa Mulungu 1 Yehova acita ufumu; dziko lapansi likondwere; Zisumbu zambiri zikondwerere. 2 Pomzinga pali mitambo ndi mdima; Cilungamo ndi ciweruzo ndizo zolimbitsa mpando wacifumu wace. 3…

Masalmo 98

Alemekeze Mulungu pa cifundo ndi coonadi cao Sa1mo. 1 Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano; Popeza anacita zodabwiza: Dzanja lace lamanja, mkono wace woyera, zinamcitira cipulumutso, 2 Yehova anawadziwitsira cipulumutso cace; Anaonetsera…

Masalmo 99

Mulungu wamkuru wacifundo alemekezedwe 1 Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke. 2 Yehova ndiye wamkuru m’Ziyoni; Ndipo akwezeka pamwamba pa mitundu…

Masalmo 100

Olengedwa ndi Mulungu amlemekeze Salmo la Ciyamiko. 1 Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi. 2 Tumikirani Yehova ndi cikondwerero: Idzani pamaso pace ndi kumyimbira mokondwera, 3 Dziwani kuti Yehova…

Masalmo 101

Davide akuti adzasamala okhulupirika nadzacotsa oipa Salmo la Davide. 1 Ndidzayimba za cifundo ndi ciweruzo; Ndidzayimba zakukulemekezani Inu, Yehova. 2 Ndidzacita mwanzeru m’njira yangwiro; Mudzandidzera liti? Ndidzayenda m’nyumba mwanu ndi…

Masalmo 102

Wopsinjika apempha Mulungu acitire anthu ace cifundo, amitundu nammverenso Pemphero la Wozunzika, m’mene anakomoka natsanulira cobnaatira cace pamaso pa Yehova, 1 Yehova, imvani pemphero langa, Ndipo mpfuu wanga ufikire Inu….