Masalmo 63
Mtima woliralira kuyanfana ndi Mulungu Salmo la Davide; muja akakhala m’cipululu ca Yuda. 1 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga; ndidzakufunani m’matanda kuca: Moyo wanga ukumva ludzu la kwa Inu, thupi…
Mtima woliralira kuyanfana ndi Mulungu Salmo la Davide; muja akakhala m’cipululu ca Yuda. 1 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga; ndidzakufunani m’matanda kuca: Moyo wanga ukumva ludzu la kwa Inu, thupi…
Davide apempha Mulungu amciniirize pa omlalira Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davido. 1 Imvani Yehova, mau anga, m’kudandaula kwanga; Sungani moyo wanga angandiopse mdani. 2 Ndibiseni pa upo wacinsinsi…
Davide alemekeza Mulungu pa madalitso ocuruka Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo, nyimbo ya Davide. 1 M’Ziyoni akulemekezani Inu mwacete, Mulungu: Adzakucitirani Inu cowindaci. 2 Wakumva pemphero Inu, Zamoyo zonse zidzadza…
Acenjeza onse alemekeze Mulungu pa nchito zace zodabwiza Kwa Mkulu wa Nyimbo. Nyimbo. Salmo. 1 Pfuulirani kwa Mulungu, dziko lonse lapansi. 2 Yimbirani ulemerero wa dzina lace; Pomlemekeza mumcitire ulemerero….
Amitundu alemekeze Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo, pa Neginolo. Salmo, Nyimbo. 1 Aticitire cifundo Mulungu, ndi kutidalitsa, Atiwalitsire nkhope yace; 2 Kuti njira yanu idziwike pa dziko lapansi, Cipulumutso canu…
Mau akuyamikira Mulungu wa cipulumutso conse Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. Nyimbo 1 Auke Mulungu, abalalike adani ace; Iwonso akumuda athawe pamaso pace. 2 Muwacotse monga utsi ucotseka;…
Davide adandaulira kwa Mulungu cifukwa ca zowawa azimva Kwa Mkulu wa Nyimbo. Pa Syosyanimu. Salmo la Davide. 1 Ndipulumutseni Mulungu; Pakuti madzi afikira moyo wanga. 2 Ndamira m’thope lozama, lopanda…
Davide apempha Mulungu amlanditse msanga Kwa Mkulu wa Nyimbo: cikumbutso ca Davtde, 1 Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu; Fulumirani kundithandiza, Yehova. 2 Acite manyazi, nadodome Amene afuna moyo wanga: Abwezedwe m’mbuyo, napepulidwe….
Nkhalamba idziponya kwa Mulungu amene anamkhulupira kuyambira ubwana wace 1 Ndikhulupirira Inu, Yehova: Ndisacite manyazi nthawi zonse. 2 Ndikwatuleni m’cilungamo canu, ndi kundilanditsa: Ndicherereni khutu lanu ndi kundipulumutsa. 3 Mundikhalire…
Za ufumu wa Mfumu yokoma Salimo la kwa Solomo. 1 Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, Ndi mwana wa mfumu cilungamo canu. 2 Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m’cilungamo, Ndi…