Masalmo 53
Kupusa ndi kuipa kwa anthu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Mahalat. Cilanidzo ca Davide. 1 Citsiru cimati mumtima mwace, Kulibe Mulungu. Acita zobvunda, acita cosalungama conyansa; Kulibe wakucita bwino. 2…
Kupusa ndi kuipa kwa anthu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Mahalat. Cilanidzo ca Davide. 1 Citsiru cimati mumtima mwace, Kulibe Mulungu. Acita zobvunda, acita cosalungama conyansa; Kulibe wakucita bwino. 2…
Davide apempha Mulungu amlanditse Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Neginoto. Cilangizo ca Davide. Muja Azift anamuka nauza Sauli, kuti, Kodi Davide sabisala kwathu nanga? 1 Ndipulumutseni, Mulungu, mwa dzina lanu,…
Davide adandaula pa kuipa kwa adani, adziponya kwa Mulungu, nalangiza ena azitero iwo omwe Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Zlrumbu. Cilanliizo ca Davide. 1 Cherani khutu pemphero langa, Mulungu; Ndipo…
Davide apempha Mulungu amlanditse; ayamika atamlanditsa Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Yonat-Elem Recokimu, Miktamu wa Davide, muja Afilisti anamgwira m’Gati. 1 Mundicitire cifundo, Mulungu, pakuti anthu afuna kundimeza: Andipsinja pondithira…
Davide apempha Mulungu amciniirize, namlemekezapo Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Altasheti Miktamu wa Davide: muja anathawa Sauli au m’phanga. 1 Mundicitire cifundo, Mulungu, mundicitire cifundo; Pakuti moyo wanga ukhulupirira Inu:…
Davide adzudzula oipa Mulungu awalange Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Altasyeti; Miktamu wa Davide. 1 Kodi muli cete ndithu poyenera inu kunena zolungama? Muweruza ana a anthu molunjika kodi? 2…
Davide apempha Mulungu amlanditse, nadzinenera wosalakwa Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Altasbeti. Mikta mu wa Davide. Muja anatuma adikire nyumba yace, kuti amuphe, 1 Ndilanditseni kwa adani anga, Mulungu wanga:…
Madandaulo ndi pempho la Davide Kwa Mkulu wa Nyimbo pa Susan-Eduti. Miktamu wa Davide; lakulangiza: muja analimbana nao Aramnabaraimu ndi Aramzoba, nabwera Yoabu napha a Edomu m’Ciagwa ca Mcere zikwikhumi…
Poopsedwa Davide athamangira Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo; Neginoto. Salmo la Davide. 1 Imvani mpfuu wanga, Mulungu; Mverani pemphero langa. 2 Ku malekezero a dziko lapansi ndidzapfuulira kwa Inu, pomizika…
Posautsidwa Davide athamangira Mulungu yekha Kwa Mlrulu wa Nyimbo, pa Jedutunu. Salmo la Davide. 1 Moyo wanga ukhalira cete Mulungu yekha: Cipulumutso canga cifuma kwa Iye. 2 Iye yekhayo ndiye…