Masalmo 43

Davide alira akhale ku Kacisi 1 Mundiweruzire, Mulungu, ndipo mundinenere mlandu kwa anthu opanda cifundo: Mundilanditse kwa munthu wonyenga ndi wosalungama. 2 Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji?…

Masalmo 44

Anthu a Mulungu akumbuke zithandizo zakale popempha cipulumutso m’tsoka lao Kwa Mkulu Wa Nyimbo; Cuangizo ca ana a Kora. 1 Mulungu, tidamva m’makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, Za nchitoyo mudaicita…

Masalmo 45

Nyimbo voyimbira ukwati wa mfumu Kwa Mkulu wa Nyimbo pa Syosyanim. Cilangizo ca kwa ana a Kora. Nyimbo ya cikondi. 1 Mtima wanga usefukira naco cinthu cokoma: Ndinena zopeka ine…

Masalmo 46

Mulungu ndiye pothawirapo anthu ace Kwa Mkulu wa Nyimbo; Cilangizo ca kwa ana a Kora. Pa Alamot. Nyimbo. 1 Mulungu ndiye pothawirapo pathu ndi mphamvu yathu, Thandizo lopezekeratu m’masautso. 2…

Masalmo 47

Mau a kulemekeza Mulungu mwini dziko lonse lapansi Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la ana a Koro. 1 Ombani m’manja, mitundu yonse ya anthu; Pfuulirani kwa Mulungu ndi liu la…

Masalmo 48

Ukoma ndi ulemerero wa Ziyoni Nyimbo; Salmo la ana a Kora. 1 Yehova ndiye wamkulu, ayenera kulemekezekadi, M’mudzi wa Mulungu wathu, m’phiri lace loyera. 2 Phiri la Ziyoni, cikhalidwe cace…

Masalmo 49

Za pansi pano nza cabe Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salmo la ana a Kora. 1 Dzamveni kuno, anthu inu nonse; Cherani khutu, inu nonse amakono, 2 Awamba ndi omveka omwe,…

Masalmo 50

Mulungu woweruza wa dziko lapansi Salmo la Asafu. 1 Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, Aitana dziko lapansi kuyambira kuturuka kwa dzuwa kufikira kulowa kwace. 2 Mulungu awalira m’Ziyoni, mokongola mwangwiro….

Masalmo 51

Davide abvomereza kucimwa kwace, apempha Mulungu amkhululukire, asamcotsere Mzimu Woyera Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide; m’mene anamdzera Natani mnenertso atalowa iye kwa Bateseba. 1 Mundicitire ine cifundo, Mulungu,…

Masalmo 52

Davide aneneratu za cionongeko ca oipa, iye nakhulupirira Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo. Cilangizo ca Davide. Muja analowa Doegi M-edomu nauza Sauli, nati kwa iye, Davide walowa m’nyumba ya Abimeleke….