Masalmo 33

Alemekeza Mulungu wolenga, wosunga zonse 1 Pfuulani mokondwera mwa Yehova, inu olungama mtima: Oongoka mtima ayenera kulemekeza. 2 Yamikani Yehova ndi zeze: Myimbireni ndi cisakasa ca zingwe khumi. 3 Mumyimbire…

Masalmo 34

Davide alemekeza Yehova womlanditsa, nafulumiza ena amtame Salimo la Davide. Muja anasintha makhalidwe ace pamaso pa Abimeleke, amene anampitikitsa ndipo anacoka. 1 Ndidzalemekeza Yehova nyengo zonse; Kumlemekeza kwace kudzakhala m’kamwa…

Masalmo 35

Davide apempha Mulungu alange otpa Salmo la Davide, 1 Tsutsanani nao iwo akutsutsana nane, Yehova: Limbanani nao iwo akulimbana nane. 2 Gwirani cikopa cocinjiriza, Ukani kundithandiza. 3 Sololani nthungo, ndipo…

Masalmo 36

Kuipitsitsa kwa anthu, kukometsetsa kwa Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide, mtumiki wa Yehova. 1 Colakwa ca woipayo cimati m’kati mwa mtima wanga, Palibe kuopa Mulungu pamaso pace….

Masalmo 37

Kusangalala kwa ocimwa kudzatha, olungama akhalitsa nathandizidwa ndi Mulungu Salmo la Davide. 1 Usabvutike mtima cifukwa ca ocita zoipa, Usacite nsanje cifukwa ca ocita cosalungama. 2 Pakuti adzawamweta msanga monga…

Masalmo 38

Davide aulula zoipa zace, apempha Mulungu amkhululukire namthandize Salmo la Davtde, lakukumbutsa. 1 Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu: Ndipo musandilange moopsa m’mtima mwanu. 2 Pakuti mibvi yanu yandilowa, Ndi dzanja…

Masalmo 39

Kupepuka kwa moyo uno Kwa Mkulu wa Nyimbo, kwa Yedutun, Salmo la Davide. 1 Ndinati, Ndidzasunga njira zanga, Kuti ndingacimwe ndi lilime langa: Ndidzasunga pakamwa panga ndi cam’kamwa, Pokhala woipa…

Masalmo 40

Alemekeza cipulumutso ca Mulungu, alalikira poyera cilungamo ca Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Kuyembekeza ndayembekeza Yehova; Ndipo anandilola, namva kupfuula kwanga. 2 Ndipo anandikweza kunditurutsa m’dzenje…

Masalmo 41

Mulungu adalitsa wosamalira osauka. Adani ndi mabwenzi amcitira Davide zoipa, Mulungu amlanditse Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Wodala iye amene asamalira wosauka: Tsiku la tsoka Yehova adzampulumutsa:…

Masalmo 42

Mtima wolira kuyanjana ndi Mulungu m’Kacisi Kwa Mkulu wa Nyimbo. Cilangizo ca kwa ana a Kora. 1 Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; Motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu,…