Masalmo 13
Munkhawa athawira Mulungu namkhulupirira Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Mudzandiiwala ciiwalire, Yehova, kufikira liti? Mudzandibisira ine nkhope yanu kufikira liti? 2 Ndidzacita uphungu m’moyo mwanga kufikira liti,…
Munkhawa athawira Mulungu namkhulupirira Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Mudzandiiwala ciiwalire, Yehova, kufikira liti? Mudzandibisira ine nkhope yanu kufikira liti? 2 Ndidzacita uphungu m’moyo mwanga kufikira liti,…
Anthu oipadi Kwa Mkulu wa Nyimbo: Salmo la Davide. 1 Waucitsiru amati mumtima mwace, Kulibe Mulungu. Acita zobvunda, acita nchito zonyansa; Kulibe wakucita bwino. 2 Yehova m’Mwamba anaweramira pa ana…
Cikhalidwe ca munthu woona wa Mulungu Salmo la Davide. 1 Yehova, ndani adzagonera m’cihema mwanu? Adzagonera ndani m’phiri lanu lopatulika? 2 Iye wakuyendayo mokwanira, nacita cilungamo, Nanena zoonadi mumtima mwace….
Munthu wokhulupira Mulungu akhazikika mtima, osaopa kutayika Mlkitamu wa Davide. 1 Ndisungeni ine, Mulungu: pakuti ndakhulupirira Inu. 2 Ndinati kwa Yehova, Inu ndinu Ambuye wanga: Ndiribe cabwino cina coposa Inu….
Davide apempha Mulungu amsunge pa ofuna kumuononga Pemphero la Davide. 1 Yehova, imvani cilungamo, mverani mpfuu wanga; Cherani khutu ku pemphero langa losaturuka m’milomo ya cinyengo, 2 Pankhope panu paturuke…
Nyimbo yoyamikira Yehova Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la mtumiki wa Yehova, Davide, amene ananena kwa Yehova mau a nyimbo iyi m’mene Yehova anamlanditsa m’dzanja la adani ace onse, ndi…
Davide alemekeza zolengedwa ndi Mulungu, ndi malamulo ao omwe Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide 1 Zakumwamba zimalalikira ulemerero wa Mulungu; Ndipo thambo lionetsa nchito ya manja ace. 2…
Kupempherera mfumu poturukira iye kunkhondo Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Yehova akubvomereze tsiku la nsautso; Dzina la Mulungu wa Yakobo likuike pamsanje; 2 Likutumizire thandizo loturuka m’malo…
Davide ayamika Mulungu pa kugonjetsa adani Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide, 1 Yehova, adzasekera mfumu mu mphamvu yanu; Adzakondwera kwakukuru m’cipulumutso canu! 2 Mwampatsa iye cikhumbo ca mtimawace,…
Posautsidwa Davide adandaulira, apemphera, ayamika Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Ajelet Hasakara, Salmo la Davide. 1 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine? Mukhaliranji kutali kwa cipulumutso canga, ndi kwa…