Genesis 41

Yosefe ammasulira Farao maloto ace 1 Ndipo panali zitapita zaka ziwiri zamphumphu, Farao analota; ndipo, taonani, anaima panyanja. 2 Ndipo, taonani, zinaturuka m’nyanja ng’ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri za maonekedwe…

Genesis 42

Abale a Yosefe afika ku Aigupto 1 Ndipo anaona Yakobo kuti m’Aigupto munali tirigu, nati Yakobo kwa ana ace amuna, Cifukwa canji mulinkuyang’anana? 2 Ndipo iye anati, Taonani, ndamva kuti…

Genesis 43

Abale a Yosefe atsikiranso ku Aigupto 1 Ndipo njala inakula m’dzikomo. 2 Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Aigupto atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife…

Genesis 44

Abalewo ayesedwa ndi Yosefe 1 Ndipo Yosefe anauza tsanyumba wace kuti, Dzaza matumba a anthuwo ndi cakudya, monga angathe kunyamula, ndi kuika ndalama za yense kukamwa kwa thumba lace. 2…

Genesis 45

Yosefe adziulula kwa abale ace 1 Ndipo Yosefe sanakhoza kudziletsa pamaso pa onse amene anaima naye: nati, Turutsa anthu onse pamaso panga. Ndipo panalibe munthu pamodzi ndi iye pamene Yosefe…

Genesis 46

Yakobo atsikira ku Aigupto 1 Ndipo Israyeli anamuka ulendo wace ndi zonse anali nazo, nafika ku Beereseba, napereka nsembe kwa Mulungu wa Isake atate wace. 2 Ndipo Mulungu ananena kwa…

Genesis 47

Yakobo aonetsedwa kwa Farao 1 Ndipo Yosefe analowa nauza Farao nati, Atate wanga ndi abale anga, ndi nkhosa zao ndi ng’ombe zao, ndi zonse ali nazo, anacokera ku dziko la…

Genesis 48

Yakobo adalitsa ana a Yosefe 1 Ndipo panali zitapita izi, anthu anati kwa Yosefe, Taonani, atate wanu wadwala: ndipo iye anatenga ana ace amuna awiri, Manase ndi Efraimu, apite naye….

Genesis 49

Yakobo adalitsa ana ace namwalira 1 Ndipo Yakobo anaitana ana ace amuna, nati, Sonkhanani inu, kuti ndikuuzeni inu cimene cidzakugwerani inu masiku akudzawo. 2 Sonkhanani, tamvani, ana amuna a Yakobo:…

Genesis 50

Kumwalira kwa Yosefe 1 Ndipo Yosefe anagwapa nkhope ya atate wace, namlirira iye nampsompsona iye. 2 Ndipo Yosefe anauza akapolo ace asing’anga kutiakonze atate wace: ndi mankhwala osungira thupi: ndipo…