Masalmo 3
Kukhulupirika kwa Mulungu Salimo la Davide, muja anathawa Abisalomu mwana wace. 1 Yehova! Ha! acuruka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri. 2 Ambiri amati kwa moyo wanga, Alibe cipulumutso…
Kukhulupirika kwa Mulungu Salimo la Davide, muja anathawa Abisalomu mwana wace. 1 Yehova! Ha! acuruka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri. 2 Ambiri amati kwa moyo wanga, Alibe cipulumutso…
Pemphero posautsidwa Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Nesmoto. Salmo la Davide. 1 Pakupfuula ine mundiyankhe, Mulungu wa cilungamo canga; Pondicepera mwandikulitsira malo: Ndicitireni cifundo, imvani pemphero langa. 2 Amuna inu,…
Matsoka a oipa, madalitso a olungama Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Nekiloto. Salimo la Davide. 1 Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga. 2 Tamvetsani mau a kupfuula kwanga, Mfumu…
Davide apempha cifundo kwa Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Neginoto, pa Seminiti. Salmo la Davide. 1 Yehova, musandidzudzule mu mkwiyo wanu, Ndipo musandilange m’ukali wanu. 2 Mundicitire cifundo, Yehova;…
Adani amzinga, Davide adziponya kwa Mulungu Syigayoni wa Davide woyimbira Yehova, cifukwa ca mau a Kumi Mbenjamini. 1 Yehova Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu: Mundipulumutse kwa onse akundilonda, nimundilanditse; 2 Kuti…
Davide ayimbira ulemerero wa Mulungu, ndi ulemu umene Mulungu acitira mtundu wa anthu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Oititl. Salnto la Davide. 1 Yehova, Ambuye wathu, Dzina lanu liposadi nanga…
Ayamikira cipulumutso cacikuru Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Mut-laben. Salmo la Davide. 1 Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; Ndidzawerengera zodabwiza zanu zonse. 2 Ndidzakondwerera ndi kusekera mwa Inu; Ndidzayimbira…
Athamangira Mulungu pothawa adani omtsata 1 Muimiranji patari, Yehova? Mubisaliranji m’nyengo za nsautso? 2 Podzikuza woipa apsereza waumphawi; Agwe m’ciwembu anapanganaco. 3 Pakuti woipa adzitamira cifuniro ca moyo wace, Adalitsa…
Yehova asunga anthu ace nalanga oipa Kwa Mkulu wa Nyimbo: Salmo la Davide. 1 Ndakhulupirira Yehova: Mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani ku phiri lanu ngati mbalame? 2 Pakuti, onani,…
Anthu ndi amabodza, Mulungu ndiye woona Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Seminiti 1 Pulumutsani, Yehova; pakuti wofatsa wasowa; Pakuti okhulupirika acepa mwa ana a anthu. 2 Amanena za bodza munthu…