Yobu 25
Bilidadi akuti munthu sayenera kudziyesa wolungama pamaso pa Mulungu 1 Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati, 2 Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye; Acita mtendere pa zam’mwamba zace. 3…
Bilidadi akuti munthu sayenera kudziyesa wolungama pamaso pa Mulungu 1 Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati, 2 Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye; Acita mtendere pa zam’mwamba zace. 3…
Yobu atsutsa Bilidadi kuti sanamthandiza; yekha nalemekeza ukulu wa Mulungu 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu, Kulipulumutsa dzanja losalimba! 3 Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa…
Yobu adzikaniza nanenetsa kuti ocimwa ambiri akhala osalangidwa. Ena ali ndi nzeru ndi cuma, koma opanda nzeru yeni yeni 1 Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati, 2 Pali Mulungu, amene…
1 Koma kuli mtapo wa siliva, Ndi malo a golidi amene amuyenga. 2 Citsulo acitenga m’nthaka, Ndi mkuwa ausungunula kumwala. 3 Munthu athawitsa mdima, Nafunafuna mpaka malekezero onse, Miyala ya…
Yobu alinganiza cikhalidwe cace cakale ndi tsoka latsopano, nalimbika kuti sanacita zochulidwazi 1 Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati, 2 Ha! ndikadakhala monga m’miyezi yapitayi, Monga m’masiku akundisunga Mulungu; 3…
1 Koma tsopano iwo osafikana msinkhu wanga andiseka, Iwo amene atate ao ndikadawapeputsa, osawaika pamodzi ndi agaru olinda nkhosa zanga. 2 Mphamvunso ya m’manja mwao ndikadapindulanji nayo? Ndiwo anthu amene…
1 Ndinapangana ndi maso anga, Potero ndipenyerenji namwali? 2 Pakuti gawo la Mulungu locokera kumwamba, Ndi colowa ca Wamphamvuyonse cocokera m’mwambamo nciani? 3 Si ndizo cionongeko ca wosalungama, Ndi tsoka…
Elihu adzudzula Yobu ndi mabwenzi atatu omwe 1 Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pace pa iye mwini. 2 Ndipo adapsa mtima Elihu mwana wa Barakeli…
Elihu atsutsa Yobu pa kudzikuza kwace, nanenetsa kuti pomlanga munthu Mulungu ali naco cifukwa 1 Komatu, Yobu, mumvere maneno anga, Mucherere khutu mau anga. 2 Taonani tsono, ndatsegula pakamwa panga,…
Elihu anenetsa Mulungu sangathe kukhala wosalungama, koma asiyanitsa pakati pa okoma ndi oipa 1 Ndipo Elihu anabwereza kunena, nati, 2 Tamverani mau anga, inu anzeru; Mundicherere khutu inu akudziwa. 3…