Yobu 15
Elifazi atsutsa Yobu pa kudzikuza kwace. Akuti, akuru omwe atsimikiza kuti ocimwa sakhala bwino 1 Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, 2 Kodi mwini nzeru ayankhe ndi kudziwa kouluzika,…
Elifazi atsutsa Yobu pa kudzikuza kwace. Akuti, akuru omwe atsimikiza kuti ocimwa sakhala bwino 1 Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, 2 Kodi mwini nzeru ayankhe ndi kudziwa kouluzika,…
Yobu atonza mabwenziwo kuti mau ao samthandiza, akana kuti sanacimwa, nadziponya kwa Mulungu. Ciyembekezo cace ndi imfa 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Ndamva zambiri zotere; Inu nonse ndinu otonthoza…
1 Mzimu wanga watha, masiku anga afafanizika, Kumanda kwandikonzekeratu. 2 Zoonadi, ali nane ondiseka; Ndi diso langa liri cipenyere m’kundiwindula kwao. 3 Mupatse cigwiriro tsono, mundikhalire cikole Inu nokha kwanu;…
Bilidadi atsutsa Yobu pa kudzikuza kwace, nanena za tsoka la oipa 1 Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati, 2 Musaka mau kufikira liti? Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena. 3 Tiyesedwa…
Yobu achulira mabwenzi ace matsoka ace, napempha amcitire cifundo, Adzitonthoza ndi Mpulumutsi wace 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti, Ndi kundityolatyola nao mau? 3 Kakumi…
Zofari afotokozera masautso amene Mulungu atumizira oipa 1 Pamenepo anayankha Zofari Mnaama, nati, 2 M’mwemo zolingirira zanga zindiyankha, Cifukwa cace ndifulumidwa m’kati mwanga. 3 Ndamva kudzudzula kwakundicititsa manyazi, Ndi mzimu…
Yobu ayankha kuti oipa ambiri amalemerera. Zooneka m’maso sizitiuza za mtima wa Mulungu 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Mvetsetsani mau anga; Ndi ici cikhale citonthozo canu. 3 Mundilole, ndinene…
Elifazi amchulira Yobu zoipa zambiri, namuuza alape, Mulungu nadzamcitira cifundo 1 Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, 2 Kodi munthu apindulira Mulungu? Koma wanzeru angodzipindulira yekha. 3 Kodi Wamphamvuyonse…
Yobu abwereza kukana kuti sanacimwa. Mulungu wosadziwika acita cifuniro cace. Kwambiri ocimwa oyenera kulangidwa akhala bwino m’moyo uno 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; Kulanga…
1 Wamphamvuyonse alekeranji kuikiratu nyengo? Ndi iwo omdziwa alekeranji kudziwa masiku ace? 2 Alipo akusendeza malire; Alanda gulu la zoweta, nazidyetsa. 3 Akankhizira kwao buru wa amasiye, Atenga ng’ombe ya…