Yobu 5

1 Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo? 2 Pakuti mkwiyo umapha wopusa, Ndi nsanje imakantha wopanda pace. 3 Ndinapenya wopusa woyala mizu; Koma…

Yobu 6

Yobu akuti ali ndi cifukwa ca kudandaula, alira kufa, adzuzula mabwenzi pa kuuma mtima kwao, apempha Mulungu amcitire cifundo 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Mwenzi atayesa bwino cisoni canga,…

Yobu 7

1 Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno? Kodi masiku ace sakunga masiku a wolembedwa nchito? 2 Monga kapolo woliralira mthunzi, Monga wolembedwa nchito ayembekezera mphotho yace, 3 Momwemo anandilowetsa miyezi…

Yobu 8

Poona tsoka lao Bilidadi akuti Yobu ndi ana ace anacimwa, anena mofanizira 1 Pamenepo anayankha Bilidadi Msuki, nati, 2 Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati…

Yobu 9

Yobu abvomereza ukulu wa Mulungu, koma okoma ndi oipa alangidwa mmodzimodzi. Masautso ace amfunitsa kufa 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Zoona, ndidziwa kuti ciri cotero. Koma munthu adzakhala walungama…

Yobu 10

1 Mtima wanga ulema nao moyo wanga, Ndidzadzilolera kudandaula kwanga, Ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga. 2 Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; Mundidziwitse cifukwa ca kutsutsana nane. 3 Cikukomerani kodi kungosautsa, Kuti mupeputsa…

Yobu 11

Zofari adzudzula Yobu pa kudzilungamitsa kwace, namcenjeza alape 1 Pamenepo anayankha Zofari wa ku Naama, nati, 2 Kodi mau ocurukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama? 3…

Yobu 12

Yobu abvomerezanso ukulu wa Mulungu, koma mau a abwenziwo ndi opanda pace; nanena za moyo wa munthu ukutha msanga 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Zoonadi inu ndinu anthu, Ndi…

Yobu 13

1 Taonani; diso langa laciona conseci; M’khutu mwanga ndacimva ndi kucizindikira. 2 Cimene mucidziwa inu, inenso ndicidziwa; Sindikuceperani. 3 Koma ine ndidzanena ndi Wamphamvuyonse, Ndipo ndifuna kudzikanira kwa Mulungu. 4…

Yobu 14

1 Munthu wobadwa ndi mkazi Ngwa masiku owerengeka, nakhuta mabvuto, 2 Aturuka ngati duwa, nafota; Athawa ngati mthunzi, osakhalitsa. 3 Ndipo kodi mumtsegulira maso anu wotereyo, Ndi kunditenga kunena nane…