Nehemiya 8

Ezara awerengera anthu buku la cilamulo 1 Ndipo anthu onse anasonkhana ngati munthu mmodzi ku khwalala liri ku cipata ca kumadzi, namuuza Ezara mlembi atenge buku la cilamulo ca Mose,…

Nehemiya 9

Msonkhano wa kusala ndi kupemphera 1 Ndipo tsiku la makumi awiri mphambu anai la mwezi uno ana a Israyeli anasonkhana ndi kusala, ndi kubvala ciguduli, ndipo anali ndi pfumbi. 2…

Nehemiya 10

Pangano lokhazikika pakati pa anthu ndi Mulungu 1 Okomera cizindikilo tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya, 2 Seraya, Agariya, Yeremiya, 3 Pasuri, Amariya, Malikiya, 4 Hatusi, Sebaniya,…

Nehemiya 11

Ena akhala m’Yerusalemu, ena m’midzi yina 1 Ndipo akuru anthu anakhala m’Yerusalemu; anthu otsala omwe anacita maere, kuti libwere limodzi la magawo khumi likhale m’Yerusalemu, mudzi wopatulika, ndi asanu ndi…

Nehemiya 12

Maina a ansembe ndi Alevi ofika ku Yerusalemu pamodzi ndi Zerubabele 1 Ndipo ansembe ndi Alevi amene anakwera ndi Zerubabele mwana wa Sealtiyeli, ndi Yesuwa, ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,…

Nehemiya 13

Tobiya acotsedwa ku Kacisi 1 Tsiku lomwelo anawerenga m’buku la Mose m’makutu a anthu, napeza m’menemo kuti Aamoni ndi Amoabu asalowe mu msonkhano wa Mulungu ku nthawi yonse; 2 popeza…

Estere 1

Madyerero a Ahaswero 1 IZI zinacitika masiku a Ahaswero, ndiye Ahasweroyo anacita ufumu kuyambira Indiya kufikira Kusi, pa maiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri. 2 Masiku…

Estere 2

Ahaswero akwatira Estere 1 Zitatha izi, utaleka mkwiyo wa mfumu Ahaswero, anakumbukila Vasiti, ndi cocita iye, ndi comlamulidwira. 2 Pamenepo anyamata a mfumu omtumikira anati, Amfunire mfumu anamwali okongola; 3…

Estere 3

Moredekai akana kugwadira Hamani 1 Zitatha izi, mfumu Ahaswero anamkuza Hamani mwana wa Hamedata, wa ku Agagi, namkweza, naika mpando wace upose akalonga onse okhala naye. 2 Ndipo anyamata onse…

Estere 4

Moredekai adandaulira Estere anenere Ayuda kwa mfumu 1 Koma podziwa Moredekai zonse zidacitikazi, Moredekai anang’amba zobvala zace, nabvala ciguduli ndi mapulusa, naturuka pakati pa mudzi, napfuula, nalira kulira kwakukuru ndi…