2 Mbiri 34

Yosiya acotsa cipembedzo ca mafano, nakonzanso Kacisi 1 Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi atatu mphambu cimodzi. 2 Nacita zoongoka pamaso…

2 Mbiri 35

Yosiya acita Paskha ku Yerusalemu 1 Pamenepo Yosiya anacitira Yehova Paskha m’Yerusalemu, naphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi woyamba. 2 Ndipo anaika ansembe pa udikiro wao, nawalimbikitsa acite…

2 Mbiri 36

Yehoahazi, Yehoyakimu, Yehoyakini, mafumu a Yuda 1 Pamenepo anthu a m’dziko anatenga Yehoahazi mwana wa Yosiya, namlonga ufumu m’Yerusalemu, m’malo mwa atate wace. 2 Yehoahazi anali wa zaka makumi awiri…

Ezara 1

Mulungu apangira Koresi alole Ayuda abwere kwao kukamanga Kacisi 1 CAKA coyamba tsono ca Koresi mfumu ya ku Perisiya, kuti akwaniridwe mau a Yehova m’kamwa mwa Yeremiya, Yehova anautsa mzimu…

Ezara 2

Maina a Ayuda obwera ku Yerusalemu ndi Zerubabele 1 Ana a deralo, amene anakwera kuturuka m’ndende mwa andende aja Nebukadinezara mfumu ya Babulo adawatenga ndende kumka nao ku Babulo, nabwerera…

Ezara 3

Limangidwa guwa la nsembe 1 Utakhala tsono mwezi wacisanu ndi ciwiri, ana a Israyeli ali m’midzimo, anthuwo anasonkhana ngati munthu mmodzi ku Yerusalemu. 2 Nanyamuka Yesuwa mwana wa Yozadaki, ndi…

Ezara 4

Asamariya aneneza Ayuda omanga Kacisi kwa Ahaswero 1 Atamva tsono a adani Yuda ndi Benjamini kuti ana aja a ndende analikumangira Yehova Mulungu wa Israyeli Kacisi, 2 anayandikira kwa Zerubabele,…

Ezara 5

Zerubabele ndi Yesuwa apitirira kumanga Kacisi 1 Ndipo aneneri, Hagai mneneriyo, ndi Zekariya mwana wa Ido, ananenera kwa Ayuda okhala m’Yuda ndi m’Yerusalemu; m’dzina la Mulungu wa Israyeli ananenera kwa…

Ezara 6

Dariyo anenetsa kuti Kacisi amangidwe 1 Pamenepo analamulira Dariyo mfumu, ndipo anthu anafunafuna m’nyumba ya mabuku mosungira cuma m’Babulo. 2 Napeza ku Akimeta m’nyumba ya mfumu m’dera la Mediya, mpukutu,…

Ezara 7

Aritasasta atumiza Ezara ku Yerusalemu akonzenso cipembedzo ca Yehova 1 Zitatha izi tsono, pokhala mfumu Aritasasta mfumu ya Perisiya, anadza Ezara mwana wa Seraya, mwana wa Azariya, mwana wa Hilikiya,…