Genesis 31
1 Yakobo afuna kwao nathawa nazo zace, Ndipo anamva mau a ana ace a Labani kuti, Yakobo watenga zonse za atate wathu; m’zinthu zinali za atate wathu wapeza iye cuma…
1 Yakobo afuna kwao nathawa nazo zace, Ndipo anamva mau a ana ace a Labani kuti, Yakobo watenga zonse za atate wathu; m’zinthu zinali za atate wathu wapeza iye cuma…
1 Ndipo Yakobo anankabe ulendo wace, ndipo amithenga a Mulungu anakomana naye. 2 Pamene Yakobo anawaona anati, Ili ndi khamu la Mulungu: ndipo anacha pamenepo dzina lace Mahanaimu. Yakobo akonzekeratu…
Yakobo ayanjanidwa ndi Esau 1 Ndipo Yakobo anatukula maso ace, taonani, anadza Esau, ndi pamodzi naye anthu mazana anai. Ndipo anagawira ana kwa Leya, ndi kwa Rakele, ndi kwa adzakazi…
Dina ndi a Sekemu 1 Ndipo Dina mwana wamkazi wa Leya, amene anambalira Yakobo, ananka kukaona akazi a kumeneko. 2 Pamene anamuona iye Sekemu, mwana wace wamwamuna wa Hamori Mhivi,…
Yakobo amanga ku Beteli 1 Ndipo Mulungu anati kwa Yakobo, Nyamuka nukwere kunka ku Beteli nukhale kumeneko: numange kumeneko guwa la nsembe la Mulungu amene anaonekera kwa iwe pamene unathawa…
Mbumba ya Esau 1 Mibadwo ya Esau (ndiye Edomu) ndi iyi: 2 Esau anatenga akazi ace a ana akazi a m’Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Mhiti, ndi Oholibama mwana…
Yosefe agulitsidwa ndi abale ace 1 Ndipo Yakobo anakhala m’dziko limene anakhalamo mlendo atate wace, m’dziko la Kanani. 2 Mibadwo ya Yakobo ndi iyi: Yosefe anali wa zaka khumi ndi…
Yuda ndi Tamara 1 Ndipo panali nthawi yomweyo, kuti Yuda anatsikira kwa abale ace nalowa kwa M-adulami, dzina lace Hira. 2 Ndipo Yuda anaona kumeneko mwana wamkazi wa Mkanani dzina…
Yosefe ayesedwa ndi mkazi wa Potifara 1 Ndipo anatsika naye Yosefe kunka ku Aigupto; ndipo Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda, Maigupto, anamgula iye m’manja mwa Aismayeli amene anatsika…
Yosefe m’kaidi amasulira maloto 1 Ndipo panali zitapita izi, wopereka cikho wa mfumu ya Aigupto ndi wophika mkate wace anamcimwira mbuye wao mfumu ya Aigupto. 2 Ndipo Farao anakwiyira akuru…