2 Mbiri 14
Asa akantha Akusi 1 Momwemo Abiya anagona ndi makolo ace, ndipo anamuika m’mudzi wa Davide; ndi Asa mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace, m’masiku ace dziko linaona bata zaka khumi….
Asa akantha Akusi 1 Momwemo Abiya anagona ndi makolo ace, ndipo anamuika m’mudzi wa Davide; ndi Asa mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace, m’masiku ace dziko linaona bata zaka khumi….
Asa acotsa mafano nabwereza cipangano ndi Mulungu 1 Pamenepo mzimu wa Mulungu unagwera Azariya mwana wa Odedi, 2 ndipo anaturuka kukomana naye Asa, nanena naye, Mundimvere, Asa, ndi onse Ayuda…
Asa apangana ndi Benihadadi, nalimbana ndi Israyeli 1 Caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi ca Asa, Basa mfumu ya Israyeli anakwera kulimbana ndi Yuda, namangitsa Rama, kuwaletsa anthu…
Ukoma ndi ukulu wa Yehosafati 1 Ndipo Yehosafati mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace, nadzilimbitsa kuyambana ndi Israyeli. 2 Naika ankhondo m’midzi yonse yamalinga ya Yuda, naika aboma m’dziko la…
Pangano pakati pa Yehosafati ndi Ahabu; afunsira kwa aneneri 1 Yehosafati tsono anali nacocuma ndi ulemu zomcurukira, nacita cibale ndi Ahabu. 2 Ndipo zitatha zaka zina, anatsikira kwa Ahabu ku…
Mneneri Yehu adzudzula Yehosafati 1 Ndipo Yehosafati mfumu ya Yuda anabwerera ku nyumba yace ku Yerusalemu mumtendere. 2 Naturuka Yehu mwana wa Hanani mlauli kukomana naye, nati kwa mfumu Yehosafati,…
Yehosafati apempha Yehova pa Amoabu ndi Aamoni 1 Ndipo zitatha izi, kunacitika kuti ana a Moabu, ndi ana a Amoni, ndi ena pamodzi ndi Aamoni, anadza kuyambana nkhondo ndi Yehosafati….
Yoramu mfumu yoipitsitsa ya Yuda 1 Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m’mudzi wa Davide; ndi Yehoramu mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2…
Ahaziya mfumu ya Yuda aphedwa ndi Yehu 1 Ndipo okhala m’Yerusalemu anamlonga Ahaziya mwana wace wamng’ono akhale mfumu m’malo mwace; pakuti gulu la anthu, adadzawo pamodzi ndi Aarabu kucigono, adapha…
Yehoyada adzoza Yoasi akhale mfumu 1 Koma caka cacisanu ndi ciwiri Yehoyada anadzilimbitsa natenga atsogoleri a mazana, Azariya mwana wa Yeroamu, ndi Ismayeli mwana wa Yohanana, ndi Azariya mwana wa…