2 Mbiri 4

Guwa la nsembe ndi thawale lamkawa ndi zipangizo zonse zina 1 Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m’litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace…

2 Mbiri 5

1 Momwemo zidatha nchito zonse Solomo adazicitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomo anabwera nazo zopatulika zija za atate wace Davide; naziika siliva, ndi golidi, ndi zipangizo zonse m’cuma ca nyumba…

2 Mbiri 6

Conena Solomo ndi pemphero lace popereka Kacisi 1 Pamenepo Solomo anati, Yehova anati kuti adzakhala mu mdima wandiweyani. 2 Koma ndakumangirani nyumba yokhalamo, malo okhazikika okhalamo Inu nthawi yosatha. 3…

2 Mbiri 7

Cibvomerezo ca Yehova mwa moto ndi ulemerero wao wodzaza Kacisi 1 Atatha tsono Solomo kupemphera, moto unatsika kumwamba, nunyeketsa nsembe yopsereza, ndi nsembe zophera; ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza nyumbayi….

2 Mbiri 8

Solomo amanga midzi yina 1 Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m’mene anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yace yace, 2 Solomo anamanga midzi imene Huramu adampatsa, nakhalitsamo ana a…

2 Mbiri 9

Mfumu yaikazi ya ku Seba aceza ndi Solomo 1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo, anadza kumuyesera Solomo ndi miyambi yododometsa ku Yerusalemu, ndi ulendo waukuru,…

2 Mbiri 10

Ufumu ugawanika pakati. Rehabiamu mfumu ya Yuda, Yerobiamu ya Israyeli 1 Ndipo Rehabiamu anamuka ku Sekemu; pakuti Aisrayeli onse adadza ku Sekemu kumlonga ufumu. 2 Ndipo kunali, atamva Yerobiamu mwana…

2 Mbiri 11

Mulungu aletsa nkhondo pakati pa Yuda ndi Israyeli 1 Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehabiamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi…

2 Mbiri 12

Sisaki wa ku Aigupto athira nkhondo Rehabiamu 1 Ndipo kunacitika, utakhazikika ufumu wa Rehabiamu, nalimbika iye, anasiya cilamulo ca Yehova, ndi Aisrayeli onse pamodzi naye. 2 Ndipo Rehabiamu atakhala mfumu…

2 Mbiri 13

Abiya ndi Yerobiamu agwirana nkhondo, Israyeli akanthidwa 1 Ndipo caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yerobiamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda. 2 Anakhala mfumu m’Yerusalemu zaka zitatu; ndi dzina…