1 Mbiri 23
Davide alonga Solomo m’ufumu, nakonza cigawo ca Alevi 1 Atakalamba tsono Davide ndi kucuruka masiku, iye analonga mwana wace Solomo akhale mfumu ya Israyeli. 2 Ndipo anasonkhanitsa akuru onse a…
Davide alonga Solomo m’ufumu, nakonza cigawo ca Alevi 1 Atakalamba tsono Davide ndi kucuruka masiku, iye analonga mwana wace Solomo akhale mfumu ya Israyeli. 2 Ndipo anasonkhanitsa akuru onse a…
Magawo 24 a ansembe 1 Ndipo magawidwe a ana a Aroni ndi awa. Ana a Aroni: Nadabu, ndi Abihu, Eleazara, ndi Itamara. 2 Koma Nadabu ndi Abihu anafa, atate wao…
Cigawo ca oyimbira nyimbo 1 Ndipo Davide ndi akazembe a gulu la nkhondo anapatulira utumikiwo ena a ana a Asafu, ndi a Hemani, ndi a Yedutuni, anenere ndi azeze, ndi…
Cigawo ca odikira 1 A magawidwe a odikira a Akora: Meselemiya mwana wa Kore wa ana a Asafu. 2 Ndipo Meselemiya anali ndi ana, woyamba Zekariya, waciwiri Yedyaeli, wacitatu Zebadiya,…
Ankhondo ndi akazembe ao 1 Ndipo ana a Israyeli monga mwa ciwerengo cao, kunena za akuru a nyumba za makolo ao, ndi akazembe a zikwi, ndi a mazana, ndi akapitao…
Davide alangiza akuru onse ndi Solomo yemwe 1 Pamenepo Davide anasonkhanitsa ku Yerusalemu akalonga Israyeli, a akalonga a mapfuko, ndi akuru a zigawo zakutumikira mfumu, ndi akulu a zikwi, ndi…
Zopereka zaufulu zomangira Kacisi 1 Mfumu Davide ananenanso kwa khamu lonse, Mulungu wasankha mwana wanga Solomo yekha, ndiye mnyamata ndi wosakhwima; ndipo nchitoyi ndi yaikuru, pakuti cinyumbaci siciri ca munthu,…
Solomo apereka nsembe ku Gibeoni 1 NDIPO Solomo mwana wa Davide analimbikitsidwa m’ufumu wace, ndipo Yehova Mulungu wace anali naye, namkuza kwakukuru. 2 Ndipo Solomo analankhula ndi Aisrayeli onse, ndi…
Solomo apangana ndi Hiramu za mirimo ya Kacisi 1 Ndipo a Solomo anati alimangire dzina la Yehova nyumba, ndiponso nyumba ya ufumu wace. 2 Nawerenga Solomo amuna zikwi khumi mphambu…
Mamangidwe a Kacisi 1 Pamenepo Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu, m’phiri la Moriya, kumene Mulungu anaonekera kwa Davide atate wace, pamalo pamene Davide anakonzeratu pa dwale la…