1 Mbiri 13

Apita nalo likasa nalisunga m’nyumba ya Obedi Edomu 1 Ndipo Davide anafunsana ndi akuru a zikwi ndi a mazana, inde atsogoleri ali onse. 2 Ndipo Davide anati kwa msonkhano wonse…

1 Mbiri 14

Cibwenzi ca Hiramu, kulephera kwa Afilisti 1 Ndipo Hiramu mfumu ya Turo anatumiza mithenga kwa Davide, ndi mikungudza, ndi amisiri omanga miyala, ndi amatabwa, kuti ammangire nyumba. 2 Ndipo Davide…

1 Mbiri 15

Davide afikitsa, likasa ku Yerusalemu, nalongosola mapembedzedwe 1 Ndipo Davide anadzimangira nyumba m’mudzi mwace, nakonzeratu malo likasa la Mulungu, naliutsira hema. 2 Pamenepo Davide anati, Sayenera ena kusenza likasa la…

1 Mbiri 16

1 Ndipo analowa nalo likasa la Mulungu, nalgka pakati pa hemalo Davide adaliutsira; ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika pamaso pa Mulungu. 2 Ndipo atatha Davide kupereka nsembe zopsereza…

1 Mbiri 17

Yehova salola Davide ammangire Kacisi 1 Ndipo pokhala Davide m’nyumba mwace, Davideyo anati kwa Natani mneneri, Taona, ndikhala ine m’nyumba yamikungudza, koma Gkasa la cipangano likhala m’nsaru zocinga. 2 Ndipo…

1 Mbiri 18

Davide akantha Afilisti, Amoabu, Aaramu, ndi Aedomu 1 Ndipo zitatha izi, Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa, nalanda Gati ndi midzi yace m’manja a Afilisti. 2 Anakanthanso Moabu; ndi Amoabu anakhala anthu…

1 Mbiri 19

Davide abwezera cilango kwa Aamoni pa cipongwe cao 1 Ndipo zitatha izi, Nahasi mfumu ya ana a Amoni anamwalira, ndi mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2 Ndipo Davide anati,…

1 Mbiri 20

1 Ndipo kunali, pofikanso caka, nyengo yakuturuka mafumu, Yoabu anatsogolera khamu lamphamvu, napasula dziko la ana a Amoni, nadza, naumangira misasa Raba. Koma Davide anakhala ku Yerusalemu. Ndipo Yoabu anakantha…

1 Mbiri 21

Davide awerenga anthu; mliri ugwera Israyeli 1 Pamenepo Satana anaukira Israyeli, nasonkhezera Davide awerenge Israyeli. 2 Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa akuru a anthu, Kawerengeni Israyeli kuyambira ku…

1 Mbiri 22

Davide akonzeratu mirimo yakumanga kacisi 1 Ndipo Davide anati, Pano padzakhala nyumba ya Yehova Mulungu, ndi pano padzakhala guwa la nsembe yopsereza la Israyeli. 2 Ndipo Davide anati asonkhanitse alendo…