1 Mbiri 3

Adzukulu a Davide 1 Ana Davide tsono ombadwira ku Hebroni: woyamba a Amnoni wa Ahinoamu wa ku Yezreeli, waciwiri Danieli wa Abigaili wa ku Karimeli, 2 wacitatu Abisalomu mwana wa…

1 Mbiri 4

Adzukulu a Yuda 1 Ana a Yuda: Perezi, Hezroni, ndi Karmi, ndi Huri, ndi Sobala. 2 Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo…

1 Mbiri 5

Adzukulu a Rubeni 1 Ndipo ana a Rubeni mwana woyamba wa Israyeli, (pakuti ndiye mwana woyamba; koma popeza anaipsa kama wa atate wace ukulu wace unapatsidwa kwa ana a Yosefe…

1 Mbiri 6

Adzukulu a Levi 1 Ana a Levi: Gerisomu, Kohati, ndi Merari. 2 Ndi ana a Kohati: Amramu, Izara, ndi Hebroni, ndi Uzieli. 3 Ndi ana a Amramu: Aroni, ndi Mose,…

1 Mbiri 7

Adzukulu a Isakara 1 Ana a Isakara ndiwo Tola, ndi Pua, Yasubu ndi Simironi; anai. 2 Ndi ana a Tola: Uzi, ndi Repaya, ndi Yerieli, ndi Yamai, ndi Ibsamu, ndi…

1 Mbiri 8

Adzukulu a Benjamini ndi Sauli 1 Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wace vyoyamba, Asibeli waciwiri, ndi Ahara wacitatu, 2 Noha wacinai, ndi Rafa wacisanu. 3 Ndi Bela anali ndi ana:…

1 Mbiri 9

Okhala m’Yerusalemu atabwera kucokera ku Babulo 1 Ndipo Aisrayeli onse anawerengedwa mwa cibadwidwe cao; ndipo taonani, alembedwa m’buku la mafumu a Israyeli; ndipo Yuda anatengedwa ndende kumka ku Babulo cifukwa…

1 Mbiri 10

Za imfa ya Sauli ndi ana ace 1 Afilisti tsono analimbana nkhondo ndi Israyeli; ndipo amuna a Israyeli anathawa pamaso pa Afilisti, nagwa ophedwa pa phiri la Giliboa. 2 Ndipo…

1 Mbiri 11

Davide atalowa ufumu alanda Yerusalemu 1 Pamenepo Aisrayeli onse anasonkhana kwa Davide ku Hebroni, ndi kuti, Taonani, ife ndife pfupa lanu, ndi mnofu wanu. 2 Ngakhale kale lomwe, pokhala mfumu…

1 Mbiri 12

Amphamvu anadza kwa Davide namtsata pomlonda Sauli 1 Anadzawo kwa Davide ku Zikilaga, akali citsekedwere cifukwa ca Sauli mwana wa Kisi, ndi awa; ndiwo mwa amphamvuwo omthandiza kunkhondo. 2 Anakoka…